Email a copy of 'Hock Enterprise incur 'huge loses' from Intercity Bonanza: Nomads turned down invitation' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Hock Enterprise incur 'huge loses' from Intercity Bonanza: Nomads turned down invitation' to a friend
U.S. Ambassador to Malawi Virginia Palmer on Tuesday presided over the swearing-in of nine Global Health Service (GHSP) Volunteers and...
Kupusa umafuna ndalama ndiye Mulungu wakupatsa lesson kuti amadziwa zomwe tilingalira angakhale sitinazinene.mwanji sunatenge 8m ndikupereka umafuna profit.hahaha kupusa
Good trial FK in business we learn not lose and win!!!
Bambo apa zawonetsa kuti mutu wanu sumagwira , mbiri zanu tava kuti ndinu munthu wopanda zelu. ndalama zimene mukuseweletsazo mukumbuke komwe zinachoka. ife timadziwa kuti bambo katundulu palibe chazelu chimene angachite chifukwa ndumunthu woti mutuwake sumayenda bwinobwino.
UNDERSTAND THAT UR IN BUSINESS AND YOU WERE WILLING TO PART WITH SOME PROCEEDS, NOT A BAD LESSON THOUGH, NEXT TIME DO SOME THOUROUGH RESEARCH, PLIZ DON’T INVOLVE ‘NETBALL ASSOCIATION OF MALAWI’ & FAM, TRY ROAD TRAFFIC FC & MRA FC, THEY’RE VERY GOOD FUND RAISERS!!!!
hahahaha! mkulu iwe ndiwe oseketsa wamva. umayeneka kupeleka 2 mita kwa anthu a khunguwo. 6 mita yinayo umayeneka kugulila materials a company yako kuti ulenge 8 mita yina. choncho mulungu ndi anthu tinakakuyamikila kuti ndiwe okoma mtima, unakagula visa yolowera kumwamba komanso business yako inakatukuka heavy.
kumpila kumachuluka zidakwa ndi mahule. thats why enafe mpila wapa malawi tilibe nawo filimu. uzichenjera mphwanga
You lying my dear
Musatinyase Apa. Mmene Munachitira Organise Competition Yanuyo Mkumayembekezera Profit? If You Wanted Money You Could Include Moyale & Wanderers To Play Together With Silver & Bullets. Si Za Civo Or Blue Eagles. Apa Zaoneseratu Kuti Ma Organisers A Trophy Imeneyi Makape, Nepotists, Regionalists & Mbuzi.
Very poor marketing research. You mean you did not conduct any prior mini-research ahead of the plans to host the bonanza? Why couldn’t you just donate the K8 million in cash or in infrastructure or any material towards the Mua School for the Blind? Was it just a ploy to gain some popularity so that you join politics in the next two years or so? The tournament’s patronage was not pathetic. You are pathetic, pronto.
SMEs sponsoring football in Malawi is a gamble, welcome to Malawi unrealities part 1
Sorry Frank. But some people smiled.
Such is life, go on with it