Email a copy of 'I did not hesitate to accept Bingu proposal for marriage - Callista' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'I did not hesitate to accept Bingu proposal for marriage - Callista' to a friend
Hundreds of people have marched in the northern region district of Rumphi to protest against the starvation of patients in...
Ndani safuna ndalama abale inu, monga mutakhala inu mungakane?
kalista ndi dhilu tu . nanga ce mangulama ku UK, CE CIMOMBO ATPITA KU uk unacita book ku hotela yhhhhel, ndi dhilutu iyi, kumangokawa anthu. kanali ka team ka azimai amenewa. wina uyu ali paseli pa CI KKKKK.
EISH AZIMAI AWA!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
god will punish all liars money was at a centre stage
Callista, usatinamizepo apa. Anamuvomera gogo wakoyo kamba ka chuma komanso kufuna estate ya ku Mitundu. Chilungamo chake umachidziwa kuti ngangayi imwalira nsanga kenako iwe utenge estate ya kumitunduyo.
Chabwino, mwayi umenewo, mawa timva awanso anena choncho kkkkk
Unakhalitsa nde kunamera kangaude…pamenepo ungachedwenso kunena kuti ndalola
She followed the money!
Pachikhalidwe chathu mukanayamba mwakana kaye wosangofikira kuvomera popeza zimawonetsa ngati kutaya chikhalidwe posaganizira zinazo. Ifenso amuna tinazolowera kuti akazi amayamba akana kaye ngakhale akufuna
The truth of the matter is that, when Bingu’s wife died, some DIPHIPHI women(women caucus) including JB and Callista, sat down and agreed to find a comforter(woman) that Bingu should marry. Now, when Callista knew about this arrangement, she went behind and entice Bingu to marry her. And Callista’s plan worked. Now this women caucus that included Kachikho, Kaliati, JB and others were not happy with what Callista as Kachikho was the one to become the comforter. Therefore, inorder to frustrate JB, Callista told the late president to suck off JB from her position as vice president, as well Safe… Read more »
good girl