Email a copy of 'In pictures: Chipuwa engages sweetheart Dinnah' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

45 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
willard Thipa
willard Thipa
9 years ago

You have set a gd example for the other players

Augustine Shaba
9 years ago

Ma palestina akukudikira pagolo

Ananganji
Ananganji
9 years ago

All the best our goalkeeper I wish you a nice marriage. Proud of you but remember that in marriage there are ups and downs.

Mdicai Longwe
Mdicai Longwe
9 years ago

Kukwatira ndi kufuna kwamunthu. Ndiye mukati Fisher akwatira liti izo ndiye zina. Ngati mwini wake akuona kuti kukhala opanda mkazi ndibwino musiyeni. A kakwatira kubereka ana ndikumazavutika inu nomwe ndi amene muzayambe kuima pachulu kutukwana. Khalani phe ngati mulibe chonena.

Hapuwani
9 years ago

Kodi a Chipuwa Malaya kukaunjika kunalibe mwavala inu blouseyo?

kumbukani Don Taulo
9 years ago

Be serious guyz…when our freind got married, that is important

King bwai
9 years ago

Nanga fisha akwatira liti?? batchala ameneyi kaya ndi chani kaya mwina adafa mkabudulamo

Charles
Charles
9 years ago

Zabwino zonse man koma takulandira ku Bullets uone zina

Trudge
Trudge
9 years ago

Kodi wavula agalu inu

Tiwonge
Tiwonge
9 years ago

Zowonadi kuti cipuwa akupita ku bullets? Tawonera kuvala trouser ya red pacinkhoswepa. Kkkkkkkkk

Read previous post:
Malawi ruling DPP revisited

The Democratic Progressive Party (DPP) initially ruled this country between 2004 and 2012 under the autocratic stewardship of the late...

Close