Email a copy of 'In support of the abolition of JCE and increased fees for Malawi public schools' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

36 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
batili la peter
batili la peter
8 years ago

its all bullshit …amene akugwilizana ndi bwanawa ndima nuckle heads coz mbalameyi yabalarika….

Nkolokolo
Nkolokolo
8 years ago

Basi kumangosunga ma xool report kuti ukalephera form 4 anthu adzadziwe kuti unapitako ku xool

mnzalero
8 years ago

bliliant idea,psle, jce z nthin.

MALAWISH
MALAWISH
8 years ago

Please ngati pali maganizo opusa chilowereni m’boma this government ndiawawa palibe zifukwa zokwanila zakuti ndikuma ika fee ku primaly xool and also ku makasegulira ttc kuti aziphunzisi azikalipila pamene pali ena otianapangidwa train kma ntchito sakulembedwa. Ngati zakuvutani you can just resign zisanafike poti anthu mkupanga ma demonstrations mukukanika kuwapanga trace anthu amene anaononga ndalama zochuluka zamtundu wa amalawi. Mukulimbana ndi kusegula ma community college pa mene mukukanika kupanga fund ma public technical colleges off coarse it is great idea kutsegula mwayi kwa anthu omwe sanapitenayo xool patali kma muku enela kumapanga balance kut chitukuko cha dziko chipite pa tsogolo.… Read more »

Adona akuda
Adona akuda
8 years ago

Now adays jce is nothing but poyamba kulipilitsa ku chipatalapa mmmm sipalibwino just imagine mmene kukumazazila kuquiz muthu kupita mamawa mpaka madzulo mwinanso osathandizidwa sikufuna kumadikila mpaka madzulo koma kusowa aaa pamenepa aboma aganizepo bwino

nation Nyirenda
nation Nyirenda
8 years ago

thats bushits : nde asiye kumatidula zimisonkho zambirimbiri……. and busy kunamizira kuti ndalama tilibe koma viwanthu tho ku ku usa nadi unenesko palije 2019 i promise u i mean kuti wako wapyaaaaa i mean whats dat….

mbuchindele
mbuchindele
8 years ago

It’s time for maneb people to make money. Azigulitsa ma certificate a form 4. Nanga munthu ukhala bwanji opanda certificate olo imodzi ukalakwa MSCE? Pitala nchitsiru inu musamubakile

KAWANU ANGUYE
KAWANU ANGUYE
8 years ago

Munthu Wakumudzi Amalephera Kugula Uniform Ya Ana Ake Atatu Ndiye Angakwanitse Kulipira Kusukulu? Kuthetsa Mayeso A Std 8 Ndi Form 2 Penapake Sizilibwino Chifukwa Ophunzira Ambiri Azichita Mantha Polemba Mayeso A Folomu 4 Mapeto Ake Nambala Ya Olephera . …….. Ndiye Popanga Zinthu Tikuyenera Kuganizira Anthu Akumudzi.Sizoti Mukathuta Mpunga Wanu Mumvekele Kupulaimale Ophunziripira.

Beinjingnetnyaxy
Beinjingnetnyaxy
8 years ago

I just wasted my preecious time reading this stinking trash! Abolishing mayeso? Vuto la dyera ndi limenelo, chifukwa inu munadutsamo kale, you dont consider the next generation. Its not an issue of emppoyment. Next mumva msce ndi diploma tathetsa tiyambira pa degree nanga si imene ikuchitidwa advertise. Signs of failed state, instead of improving, you abolish. Atleast if the money were put to prudent use, we could have a reason to understand, but with this political elite abuse of our hard earned taxes, it is better I have my certificate than to save money only for somebody to plunder. Nosense!!!!!!!!!!!

harr
harr
8 years ago

in zimbabwe,jce waz abolished in the year 2000.the same wth other countries who were economically stable by that time.they z nthing wrong wth the decision.how do primary schools go by it when learners fail?they are forced to repeat.the same principle applies.oh Malawians let us face facts and stop politicisng everything

Read previous post:
Jamaican artist Busy Signal confirms Malawi show: Sand Music Festival

Amidst skepticism among Malawians regarding Sand Music Festival’s claims that they had secured the signature of highly rated Jamaican artist...

Close