Email a copy of 'Inkosi Gomani V dethroned: Youthful Ngoni Paramount chief accused of despising royals' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Inkosi Gomani V dethroned: Youthful Ngoni Paramount chief accused of despising royals' to a friend
World soccer governing body, Fifa has given Malawi an Okay to play their forthcoming World Cup qualifiers against Tanzania on...
The politcs of our new world, even ophinzira a ambuye yesu ankamuwuza yesu kuti asathandize mzimayi wina coz sanali muyuda Meaning Anthu ozungulira atsogoleri anthuwa ndamene amalakwisa, go to Matt 15 vs 3….
Inu tikufuna mafumu achinyamata ozitsata who can capture on iPad. Gomani V ndi dhilu
Anthu a nkhuli ndi choncho basi
Osamupangra nsanje nd kaduka coz dats nt a big deal..dnt rush t conclusion
Iwe dingswayo iwe ndi titus iwe choka. Kodi ufumu wa chingoni umatero? Chokani akaduka inu.
amene mwamuyikayo adali kuti nthawi zonse?osamapadelo chifukwa chakaduka,ma ufumu makono akufuna ana ophunzira bwino oziwa technology wawa,zinatha kalekale zolowetsa mfumu zochita kudinda posayina mwanvaàà……..,m’bwezeleni mwana mazira angakule bwanji mngake
amukhomerera2,koma sibhoo
Reaching at that extent means the chief is sturbon. He is a man of his own words
Anamudziwa mimba mwa amayi ake asanabadweeee .ndipo amake anali anzeru analora kulowoledwa enawo amawo nzeru zinawathawa bwenzi umfumu uli wawo .mulekeni swati mukusewera ndi mwana wa mulungu akukathani ndinthu kani munatenga chisoti chake chija ndi inu eti back to sender mulungu wa swati ndi mai malinki ndi wamoyo.
At 20 , he is stl young and he really needs more and more advise bt what is happening here is that politics is ciculating in this chieftaincy. Why ru chasing him now instead of advising him kwaine sindikugwirizana nazo kuti ndiwosamva coz Paramount is not doing things payekha without seeking advise from his advisers? VP, plz,plz,plz help this young Paramount, ayitaneni onse mukhale nawo mukachipinda komata kuti iyi ithe coz nkhaniyi siyochititsa manyazi mtundu wa Gomani okha ayi koma ikuchititsa manyazi mtundu wa Malawi.