Email a copy of 'Japanese player Nakamula acclimatising to Malawi weather: Hailed by Coach Chamangwana' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Japanese player Nakamula acclimatising to Malawi weather: Hailed by Coach Chamangwana' to a friend
The Protect the Goal High HIV Cluster Project is expected to be launched on high note on Saturday afternoon with...
koma ameneyi ndiwampira?
Athera kuno njomba zakezo
Yho!!!, football? Tchin.
Ma tials mpaka chaka muwuzeni chilunga bwa ngati zavuta
Mukuona ngat munthu mmodzi angatukure masewera a mpira a Coach? Ameneyu mukwanisa kumulipira ngat mukukanika kuwalipira anyamata amomwemuno bwa? Mwasowa zochita et?
Wathu wathu ameneyu, enanu muzikasaka njira zobwezera 72million za ngongole ija.
it should be the other way round.malawi players playing in japan not this nonsense
Elijah Phimbi? Kuzolowera ma L instead of ma R eti? As in light leg and reft turn.kkkkkkkk Its Nakamura not Nakamula. OK?
Osamangoyamikilatu mphwepmhwa acoach kkkkkkkkk
ANABWERA KUDZAGULISA MA GALIMOTO OSAT ZA MPIRA