Email a copy of 'Jappie’s positive spin on Malawi UN delegation fails: State House refutes airline story' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

41 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mbowe Mulambia
8 years ago

Pali chinsiru China chake akuti SK changolemba manyi oka oka

kate
kate
8 years ago

I AGREE WITH NO 34. WE HAVE A SICK PRESIDENT INDEED. ACTUALLY WE HAVE PRESIDENT WHO IS INCAPASTATED.

S. K
S. K
8 years ago

Mulimonse tinganenere nenani koma zoona zake ndizoti ufulu olemba kapena olankhula wanyanya. Zinazi tikuonjeza. Mpaka tifika polemba ndi mtundu wa pant amene a pulezident avala. Some of what is being written will never solve the problems of malawians. Kodi Kamuzu poyenda zinkakhala bwanji? Inu a Chakwera mudalipo mukudziwa. Nanga a Bakili zinali bwa? Bingu? A mai ndie amangokuimbani kuti ndege andilipilira. Zopusa. Azungu mukuchita kuwapembeza ngati mulungu wanuwo akamaenda zimatani? Mbuzi za wanthu mwatani kodi?A malawi nsanje. Musieni munthu alamulire akalephera 2019 tikumana. Zoti anakuberani mavoti zisiyeeni nkupusa kwanu. Amakuberani mulikuti? Ngati amakuberani ali kunja kwa boma ndie kuti nditulo… Read more »

Ethurama
Ethurama
8 years ago

Jappie ameneyo ndi winawake waku lweni kwa a chiheni ku lura,zasukulu ekhoto tikambabe.

Kawonga
8 years ago

Some minstrs fit well in the shoes of ministerial positions, but pipo like jappie sindikudziwa kuti adachoka kuti amapanga chani? Seem to be parked ata wrong place and wakwera yolakwika

Gwamba
8 years ago

Bodza Limeneri Bwanji Kodi? Which School Did You Go (Dpp) Guys? Shame!

Nankununkha sadzimva
Nankununkha sadzimva
8 years ago

Kodi sizingatheke kuti azungu abwerenso adzatilamulire. Chifukwatu anthu akude mwina kupatulako Kamuzu Banda palibe ndiwonapo ine. Nanga izi zikhala nduna? Kununkha ngati mtudzitudzi.

Praise
Praise
8 years ago

We have no president in Malawi. If we do, then he is so sick that he is failiing to control the affairs of the country.

Tili Chenene
Tili Chenene
8 years ago

I need to know Japie’s level of education and his field otherwise he seems mentally and intellectually challenged lad

Kingman
8 years ago

Eee zovuta kumvetsatu Wawa

Read previous post:
MCP welcomes academician Dr Sikanda in its fold

Malawi Congress Party (MCP) is strengthening its membership base in the north and has seen academician Dr Bellings Sikanda joining...

Close