Email a copy of 'Joyce Banda dismisses Mutharika’s ‘olive branch’ mantra: 'I face imminent danger in Malawi'' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Joyce Banda dismisses Mutharika’s ‘olive branch’ mantra: 'I face imminent danger in Malawi'' to a friend
There has been mixed reactions to this year’s Independence Day, with analysts and social commentators giving different views on K300...
Ndikuti tinavotera Maui mean vs mbava ya 93 billion musandinyanse mulungu akukulangani pokubweretserani mabvuto osiiya
Tinavotera amayi koma a spp anachita ncashgate ngakhale mavoti chifukwa chair mpaka lero boma ili silikulongosoka mulungu wakwiya
Mmmm,munachita nkhaza kwa anzanu amai lero mukuthawanji
koma yah! amatha kuphika nkhani, koma zosaphwa kkkkkkkk! zochita kununkha chiwisi!
the strongest woman in AFRICA , about to pee in her pants with fear! kkkkkkkkkkk! of her own making!
ati kufuna kuti dziko liziganiza za mabi, mmalo moganiza zittukuko ku Malawi kuno, tili pa liwiro, dziko layaka moto chitukuko!
kkkkkkkkkkkkkkkkk! misala yayamba akatero. kapena majini
Tinene zoona, Joyce Banda akuopedwabe, I admire this lady. Plz dzirombo inu dza DPP ndi yemwe akumwa Tea ku State House. Listen to me very well, LEAVE AMAI ALONE, isaid LEAVE HER ALONE, i repeate LEAVE JOYCE BANDA IN PEACE once agai LEAVE HER ALONEEEEEE
Peter osalimbana naye mumusiye iweyo joyce unaononga zinthu ukangobwela ufikira unyolo
God, take care of Joice Bandas life return to sender all swords rising against her in Jesus name i pray , Amen. Amai plz don’t come now. Moyo ndikamodzi.