Email a copy of 'K22 million ‘cashgate’ at Limbe Leaf Tobbaco: Police quiz suspects' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'K22 million ‘cashgate’ at Limbe Leaf Tobbaco: Police quiz suspects' to a friend
Barbara Bush, co-founder of the Global Health Corps and daughter of former U.S. president George W. Bush, during her visit...
Source yakhani yabodza yadziwikatu. Nkani ndinsanje, dzina la source Li ndi Pilirani Khungwa amend anapanga graduate limodzi ndi Tiya. A Pilirani nkhugwa omwe anakhala akuyagana nthito kwa zaka ziwiri pano akugwila nthito ku limbe leaf ngati secretary. Nthito ui adawathandiza kupeza ndi Tiya. A Pilirani chongoona zawo akuchita bwino nsanje, mutu ku zingulila. Adagwilozana ndi nzawo Francis Belekanyama omwe akugwila ku limbe leaf ngati HR Clerk, a bamboo ake ndi a Belekanyama omwewa dzina lawo linanukhila pagono nthawi cash gate. Iwowa amalandila 90000 pa mqezi koma amwakwanitsa ku samara banja ndi kuzilipolila masters degree ku amity university. A Pilirani Khungwa… Read more »
Wabodzabiwe… U think u can convince us?? Hahahaha, wagwidwa wagwidwa basi.
Koma mwana iwe ndiwe mbava ine ndimadabwa kuti limbs leaf osamangako sukulu kani ndalama zake umadya ndiwe …….ana a achikumbe akusowabkophunzila mulungu akulange ndithu
Mitima yanu iphwe. Poti anakukanani Chibwenzi. Mwayamba kupanga digress issue. Nkhani si uhule kapena zovala zache nkhani ndiya kuba. Pepani nonse omwe munakanidwa. Ps. not everyone living in Ireland ndi hule. Uhule uli mu Lunzu , mu ma chalitchi anu omwe mumapita for entertainment purposes. . Chavuta ndi umphawi chifukwa munthu yemwe anapita ku University sangamasauke to the point of embezzlng ma funds. This is a sign of the end of the age. Aliyense adzikala lawless. Ngati anthu olamula akuba ndiye munthu wamba. PEZANI ZOCHITA . Mbava zili ku capitol hill
ndaniyo ndaniyo safuna yeesu.ife tonse tili pano tifuna yesu.singing
Number 48 Golomoti is saying the truth. Anthony Kawinga 47 has written that comment out of frustration. Unachotsedwadi utaba ku catering ndiye ukufuna uname chani pano. Tchula yemwe amabayo ngati usali iwe emwe ndi nzako uja anakuchotserani limodzi. Munthu osathokoza iwe. Unachotsedwa ku KA Senior Staff Club utasokoneza makobili kukupititsa ku catering kumenekonso unaba. Ndiye uzinamiza anthu pano. A Fiscal adzayambire iwe.
Dear Tiya,
I am not surprised you have done this,Your capableof doing a thing like this ngati unandikana ine chibwenzi ku CHANCO kuba ndalama ndikachaninso.Komano inva izi Company yasiyanandi boma Company amamanga your very young my dear this is not the way we start life or a career.Asakulimbitse mtima aise akumanga zaka zake ndi ten kumapita kutsogolo.Sorry komano.
Ine wako,Mahope akale
by the way i like the way you look it makes my heart thrill with love
Am told she is fired now akumenyera Milandu pano koma oba nkhuku alikundende koma dziko ili limakonderadi
Another tobbagate Malawi at its best.Muisova mwakula mwatha.
Bad recruitment by Limbe Leaf, there were experience and qualified candidates but you settled for her. Gabadge in Gabadge out. Most institutions suffer becoz they look for cheap people and the one can easly manupulate. Akuoneka nkaladi nzanu muisova.
Is the way Malawi should go? I think we have started playing doughs who wins and who loses the game. What Ms Lipenga did is just a continuation of the cash gates currently under way.