Email a copy of 'K513m cashgate suspect Chirwa pleads guilty: Links more building contractors in the looting' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

88 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Blessings suzyo khonje

Malawi a poorest country people r stealing its resources shame lets sweat to find.

Blessings suzyo khonje

Shame on our country tikuvutika ngati silakwathu mayo ine mbava izi bwanji zibwele mustadium tizipange shariah law.

NVM
NVM
8 years ago

Hate messages should be edited. How can people of the same country be so bitter with fellow country men because of their tribe. ATumbukawo ndi anthu created in the image of God. If you met woyipa don’t generalize. Kulikonse kuli woyipa ndi abwino.

Denguzman
8 years ago

Mbava zeni zeni zimachokera ku Southern Region makamaka the Lomwe tribe. Mtumbukayu anamputsisa ndi Namata thats why he is not afraid to tell khoti zoona zokha zokha koma nditha kumutenga kukhala mmodzi wa Atumbuka opusa kwambiri.

Hotnes
Hotnes
8 years ago

This country will never have a Tumbuka president so that all you fools can take the blame of the prosperous oops disastrous Malawi so that at one one point you will be left with no choice but accept a Tumbuka leader to save your pathetic country from oblibvion.

Totty
Totty
8 years ago

Nonse onyoza yet you claim to be religious mukuzinyenga. repent.

mohammed malinga
mohammed malinga
8 years ago

tiyeni nazo onse omwe anatenga gawo kumbali yokuba ndalama za boma akalowe chifukwa sakangowasiya chocho mtundu wa amalawi ukuvutika pomwe anthu amenewa anangotyolera ndalama mtumba mwawo.Amakonda aliyense Mulungu wakumwamba.Ndipo boma litengeko gawo kuti every 1 year azipanga kalondo londo kuwona mmene chuma chayendera ngati zagwrizana ndi budgert yawo

Balamanthu
8 years ago

Mwini filimu anali Namata.Bwanji simumatha kuwerenga nkhani yachimvekere

Bikiloni Nachipanti
Bikiloni Nachipanti
8 years ago

Shaaaaa.. Koma Atumbuka ndi Alomwe mukupanga zoopsya pa Malawi pano… And munthuyu akuti akuchita kusankha ndende yomwe akakhale.. He wants Mzimba Prison… I pray that this man goes to Maula Prison.. His greed should save him

Mbuya
Mbuya
8 years ago

Those who r saying about Tumbuka’s u r follish dats kusakhana mitundu we r all Malawians

Read previous post:
APM tours sugar factory, Malawi Mangoes project in Salima: Underlines GBI as key component of development

President Arthur Peter Mutharika has reiterated his government's commitment to see to it that the Greenbelt Initiative GBI) becomes the...

Close