Email a copy of 'Kaliati, Saonda slur Chakwera again: ‘Abandoned church for selfish political interest’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

104 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Phela Endaba
Phela Endaba
8 years ago

Atsogoleri amene (a Kaliati ni anzawo) akutiuza kuti kundale (DPP) kuli asatanic (asatana) okhaokha; akuba, akupha ndi opondereza. Dr Chakwera achita ngati kukawapezerera kumeneko ndipo akuyesetsa kuthamangitsa asatanawa m’ndalemo kuti atuluke mulowe anthu a Mulungu (oimira anthu ozunziwa, osauka, oponerezewa ndi olira kuti abweretse mtendere). Kodi nzoona kuti anthu a Mulungu monga ma Bishop adzikhala abwino akamangodzudzula boma ndi kumawakaniza kuyendetsa bomalo? Tiyeni tichite chilungamo apa. A Chakwera ngati mzika ya dziko lino ali ndi ufulu kuchita nawo ndale ngakhalenso kuyendetsa boma kumene moopa Mulungu.

Gulugufe
Gulugufe
8 years ago

Koma kodi akunama anthuwa? Chakwera sanasiye ubusa kukayamba ndale?

Pensioner Wosalipidwa
Pensioner Wosalipidwa
8 years ago

Kaliati would have done better by telling her boss to pay civil service pensioners. Rantings of this kind only help underscore the fact that the country is running on pause. The president was there and enjoying while pensioners remain unpaid. A God fearing leader would do better than this DPP clown.

Mbwiye
Mbwiye
8 years ago

OFUNIKA KALIATI AZITHANA NDI JESSY NDI LUNGUZI. ONSE OYANKHULA KUNYA. AZITHANA OKHAOKHA.

Balamanthu
8 years ago

DPP ndi chipani chotembereredwa.See what will happen to it.It has no substantive issues to talk to Malawians and thats why they waste their time to castigate others rather than tackle issues.Kaliyati zimene amachita akuyesa enafe sitiziwa.

paulos banda
paulos banda
8 years ago

Kaliati ndiyo njoka akuyinena Chilimayo.

Manyaziulibe
Manyaziulibe
8 years ago

Cheap politics osachita manyazi bwanji .

Pika wa Cashgate
8 years ago

Alomwe musatinyanse apa. Mind your prostitution business and stealing.

Hamu
Hamu
8 years ago

From primary teacher to politics who condemned you?

Malani Phiri
Malani Phiri
8 years ago

May I take this oppotunity to alert the Inspector general of police on the conduct of some polece officers in area 24 theres a notorius gang leader there similiar to the one of the area 36 one his name is WENI….Over the weekeed i was attending a funeral of one of our collegues I was disturbed to hear the senior block leader lamenting over the conduct of this notorius gang leader of military ghetto .Pliz do something and investigate more.Your officers in area 24 are corrupt.TIP OF AN ICE BERG

Read previous post:
Malawi VP Chilima pleads with DPP officials against castigations

Malawi Vice President Saulos Chilima on Sunday appealed to ruling DPP party officials to stop castigating opposition members during rallies,...

Close