Email a copy of 'Kaliati says wives not ‘baby-making machines’ as Malawi commemorate World Population Day' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Kaliati says wives not ‘baby-making machines’ as Malawi commemorate World Population Day' to a friend
Teargas dispersed by police officers outside the Kamuzu Stadium in Blantyre on Sunday forced a TNM Super League game involving...
Kkuswana nkosayamba
Ngati chibelekero chanu a kweni chidavunda kaamba kotaya mimba asiyeni anzanu abeleke
Mavuto aliko ndithu,kibeleka ana koma osawasamala,kumagona ndi njala koma kumaganiza zomangobelekabe.eish.
Ine wanga Pano ndiye akukwawa nayo ya ma twins.Very soon will be popping out.Chakudya ndili nacho.Ndimalima kwabasi.We need to fill this.Malawi singazadze.Life span yaku Malawi ndi 40.If u reach 60 call yourself a lucky person.
Azimayi ena ukamangogona nawo amakakulengeza kwa azinzawo kuti ajanso ndiye kaya a neighbour atenga yachiwiri ife tikungokhala.Space ikatalikitsa azakhali ali muzatenge zisamba kumudzi mwina zikuvuta.Ndichifukwa enafe tikayamba kusinja machine sitisiya.Mwamva akweni?
A Malawi ndife opusa kwambili-Timangobereka ana without limit. Boma lilibe policy pa “Family Planning”.
Eyewitness I will assume your brain is backwards hence your backward thinking. If a woman stays at home to look after children u think that’s not a job? Men are able to go to work coz they knows are lest assured that the children are being taken care of indirectly the woman also contributes to the finances by saving childcare money etc. Another thing is that, not all women prefers staying at home. Some men are insecure and suffers with inferiority complex as the result, they prefer their wives to be staying @home……blablabla
Ine pano ndikufuna mapasa kanayi, bola moyo osalesana ayi, paja anati tichuluke ngati mchenga ndiye ngati Bible malemba alimo ife ndife ayani kuleka. Kodi A kaliati inu paja
muli ndi ana angati?
By the way how many children is she having?
Kubeleka ndi kosayamba, amene asafuna asiye.