Email a copy of 'Karonga traders protest against MRA conduct ' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Karonga traders protest against MRA conduct ' to a friend
Carlsberg Malawi has launched the ‘my country my Carlsberg’ promotionac, in selected outlets, in the Southern Region which promises to...
Indeed the Malawi government urgently need to review its customs methods, Malawi is a poverty stricken state emanates from a significant low rate of employment and poor level of education, rather the government should show gratitude the effort by its citizens to skew the poverty line through enganging in various businesses activities and migrating to other countries with better economy.
utsogoleri wa anthu ophunzira umayenda chonchotu.
Amalawi tikadali ndi khalidwe la usamunda, ntchito nkumapondereza basi, a MRA siyani kutibera, ngati umphawi wanu umene mulinawowo ndeno mufuna muthese kuzera mwa anthu a business ifeyo ngati anthu a Ku Karonga sitilola, ndinu makape kwabasi, katundu woti walowa kale mu shop, inuyo kumafunanso ndalama zina pamene pa border analipidwa kale pamene akampanga check, ngati zili choncho, musekenso ma ofesi apa border, zikuwonetsa kuti anthu amene munawalemba ntchito paborderpo simuwakhulupilira ayi.
Za Ku Karonga tatopa nazo. Bwanji kodi?
thats taxgate nkana amalemera anthuwa kumalimbirana posting yaku border……..all that doesnt go to mg1 account…..day light robbery eyaaaaaa
Akufuna ndalama za zero aid budget kuti ALOMWE apeze poyambira.
Is that small business friendly govt? How many taxes are they going to pay? MRA should start doing that to the whole country. We have many borders and their towns, so MRA start going to the centre and south as well otherwise people will start saying it is dpp govt’s hatred of the north that is instigating these taxes!!!! Then Karonga will be very troublesome. I do understand the govt’s motive, income tax should be paid by everyone who is receiving an income. They should start with big businesses as well!! My worry is if these MRA guys are collecting… Read more »
Zikutero pa kg tumalana
Honestly speaking a Malawi timapereka misonkho yambiri. Imagine the hassle we encounter pa border and as if that’s not enough timasonkha mjira kumapatsa a MRA pa Kaporo, Chitimba Jenda and at times timawapezanso pa Kanengo. We are forced to do this chifukwa timakhala tinatopa komanso kupa further delays and unnecessarily penalties by MRA> The officers take advantage and charge mosayenerera. Munthu kutenga K200,000 kukaguka katundu pa border kulipiranso mwina around the same amount. Kodi business yanji munthu ungapange kuti ndalama imeneyi ituluke? Anthufe tikuvutika and boma silukuthandiza a Malawi kutukuka no wonder Chinese and Indians have taken all small businesses… Read more »
Is that how the new “budget of subsidies” going to be implemented? Koma kumeneko!!!