Email a copy of 'Kaunda rescues Nomads to return to summit: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Kaunda rescues Nomads to return to summit: Malawi TNM Super League' to a friend
Malawi former president Joyce Banda has been handed an award for for being a tireless advocate for Womens rights ....
musalimbane ndi asu pangani zamahule basi nyerere zangazo zisiyeni
paint the goalposts please
Zandibanda man! Zandibandaaaa! Imeneyo ndi nomaaa wawa. Ine kumva kukoma kwabaxi
kumwa wamkaka bas
Atsu ali kuti ?a malawi kuchemelera zopusa timatha kusitha manyi kubwera bread ndikuchemelera Atsu ndi manyi enieni.bt don’t worry neba u hav done it,Blue Eagles is one of de best club in malawi or even we(BB)neba imativutitsa all de best neba bt osamakweza kamba mutengo this is football okufa sakudziwika neba kkkkkkkkkk.
Not bad Tinali mchikangawa Team blue 4 lyf…………….!!!!
ngati iwe udadilowetsa ndi anthu 10 pa zomba what more with the giants like KB and Blue Engles, samala umapita kumene kwatsala tchile.
Welldone boy,its not bad,kunali ku chikangawa,pa 2wks 8poimts on away games.NEBA TAZIYAMIKA MSANJE BWANJI.WODZA MANOMA WODZA
Ukayesa zocheza lero waziona, pepa neba mawa zidzayenda. Asu azipita asanaononge zambiri. A Nyasatimes tasewera 6 games ndife awa asewera 7 games ndipo Blue Eagles yasewera 8 games.
Bravo nyerere two points away is beta van none o days are not sandes noma woyeeeeeeeeee