Email a copy of 'KB inflict Nomads major title blow: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'KB inflict Nomads major title blow: Malawi TNM Super League' to a friend
It is God’s intention that His children must be free from all powers of the enemy. There are so many...
Pepa neba. Komabe uchitepo kanthu, ukutichititsa manyazi. Nanga ungokhala pachinyezi pomela china chili chonse? Mwina utayenda mwa anthu kuti uwone vuto ndi chiyani. Nanga nkutani?
bb wamkaka tikumwa hihih sorry neba
Bt nomads steal remain nomads
chikho chili m’manja a bb dats all.
nyerere womwewo kuti wawa!!!
Ngati simumaluza intercity mudatenga shame on u.
Which team this yr won the cup, is manoma why not agd team where were u? u lost on intercity shame o u!?
Komano kumayankhula bwino ntchito ilipo imaluza madrid osati kuluza noma ndiye kuti zachilendo masiku sakoma onse komanso tikaluza kumavomereza inu mukati amakuberekani ref how many penaltiens u hv given through favour of ref.
Nyelele zinali kale, pano iiiiii!……
Pepa neba. Paja iwe umadalira games in hand, tye nazo usova. How many games in hand watsala nawo? One thng u must do: either upepese game anakubereka ref ija against eni mpira pa flames pano or usinthe home ground. Apo bi, sudzawina game pa Kamtsitsi stadium. Malangizo aulele awa, ziri ndi iwe kuwagwiritsa ntchito kapena ayi. Red lions ikukunkhundidwa lero ndi mapale, tsoka ndi loti idzabwezera mkwiyo pa iwe mu kota fainolo ya Std Bank unless umupemphe Walter kuti akusinthire venue.