Email a copy of 'Kids for K150m cash ‘traders’ jailed in Malawi' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

14 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
wakukayawakukaya
9 years ago

Ku Thyolo kumeneko.

hoitty
hoitty
9 years ago

Tenant amagona nkumalota 120 million? Eee akanatukuka modabwitsatu. Kenaka akanagulitsa akazi akeo kuti agule Namiyo village yonse awapirikisemo abalache asalemo ekha. Kuteroko akaona anthu a ma estate ali amenewa amagula anthu. sagula anthu ameneo chifukwa chake anakatenga mphawi iwe kuti,uzialimira atukuke nawe ugulr wayilesi uzikasokosa nao ukanka kumuzi

Khodzombwe
9 years ago

Zodziyamba dala akuchepetserani zakazo kuli
Bwimo aknati mukakhale mukunyauda kundende moyo wanu wonse akhwrintotonu.

w.moir
9 years ago

that’s killing deserve death sentence

weddington kamanga
9 years ago

Chilango chachepa apa¤

Tnt Dynamite
Tnt Dynamite
9 years ago

Matenanti Afodyanu,achewanu Ndinu Anthu Owopya Kwambiri. Fodya Mutibele,mwakwatiranso Our Sisters,mumawabeleketsa Ana Chaka Ndi Chaka,without Kulera,kenaka Mwayamba Kugulitsa Ana Ngati Mbuzi.Stupid,you Deserve Death Penalty!!

yontho
9 years ago

winawu siumphawi okha koma uchitsiru. Just imagine kumatengela za maiko ena nkumapha ma albino kuti akagulise ziwalo zawo. No sense.

kadamanja
9 years ago

Nenani kuti atumbuka tiwone apa. Mwachoka uko kuyipitsa anzanu.

flandes
flandes
9 years ago

Such unhuman behaviour some. Animals we call people

mary
mary
9 years ago

teach them a lesson!

Read previous post:
South Korea donates K71m to Malawi disaster – Ambassador Ngwenya

Malawi’s top envoy to Japan who also doubles as the country’s envoy to South Korea but resident in Tokyo, Major...

Close