Email a copy of 'Kinnah inspires Mzuni to beat Wanderers 3-0: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Kinnah inspires Mzuni to beat Wanderers 3-0: Malawi TNM Super League' to a friend
Kasungu north east legislator Wakuda Kamanga on Friday caused a political storm in parliament when he suggested that a Government...
Mmmmhh just wait Neba iwenso sunathane nayo Mzuni, samala polankhula !!!!!!!
wadziona neba umayenda mbali kkkkkk
Its Part ov Life noma woye! (I love Noma)
Komanso iwe reporter I think in football terminology its not called scoring a “double” but rather a “brace”, otherwise we still got the idea.
Huuuuu Kholiwo(2) Kinnah kinnah chani inu. Khaya analephera ku SA/ Swaziland komabe neba wamenyedwa basi kkkkkkkkkkkkkkkkkk. Bola panthanaziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
kinnah, mwayamba makola chomene. Vwilani mateam ghakwithu kuno .mpoto nayo yiwöneske chamuna.
A MZUNI apulumukira kuti Sulumba ndi Sanudi munalibe. kkkkkkkkkkkkkkkkkk Ayayayaya!
akuluakulu,mpaka kumenya mapuleya.ndamva kuti kaliati wapezeka ku zolozolo kkkkkkkkkkk iwe yeliya kananji mufumisyemo kaziputa!
Pano munaphunzila.muziyendabe ndi refree wanu uja kkkk
Sono ndiye tiziyambila pati kuyankhulano.uku ndiye kuluza kwa matamano.mufuna tipumile pati.kulibwanji osamapanga training kumangopita ku game.nanga simwagwilizana kuti ma game onse muluze.A Kananji vomerezani kuti simumatha.Osman akuwononga team.tangogivani ma game asalawa,perekani mapoits asalawa tisapitilile kumva kuwawa.tikusowa chonyoza.