Email a copy of 'Learners match to district education manager's office over school committee' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Learners match to district education manager's office over school committee' to a friend
Champions Nyasa Big Bullets will face old time rivals Mighty Be Forward Wanderers in a Charity Shield on April 2...
eissssssssssshhhhhhhhhh ana alusa awa
ndiye inu a HR a pa Salima mukunena kuti mufufuza, muwapatsa anawa feedback, ndiye liti limenelo, chimangacho a committee wo atanyamula kale kupita nacho ku nyumba kwawo. olo muwapatse feedback anawo, chimangacho anzanuwo abweza? Iwowa a committee ana awonso sasonkha ndalama zimenezi, just becoz they are in the committee, ndiye azidyera pamutu pa makolo ena eti/ Choncho nkumanena kuti ana asukulu alibe khalidwe opanda khalidwe muli inuyo? Ndiponso osachita manyazi mpakana ana a primary kumakuchitirani match? what a shame!!!! mukona ngati anawo osapenya eti? Inutu mukunama, muonekera pa ntunda simunati. Mukatenge msanga chimangacho muwaphikire anawo phala. Dzuwa lakutenthani ku Salima… Read more »
Kuba ndi corruption konsekonse
investigation has to be done immediately. Kuba basi!!!!!!!!!!!!!!!.
Kungoti boma liyambitse kulipilitsa primary education, mumva momwe anthu okuba omwe akupindula ndi ma school collections amenewa atakanire ,nkumati amalawi ndi osauka sangakwanitse,chonsecho akufuna Iwo aziba like that.