Email a copy of 'Leticia Matache crowned Miss Lilongwe: Student of Pentecostal Life University' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Leticia Matache crowned Miss Lilongwe: Student of Pentecostal Life University' to a friend
Malawi national football team , the Flames, intensified their training on Tuesday at Chiwembe Technical Centre in Blantyre ahead of...
Ma organizer a zimenezi mungoleka kumapangitsa mpikisano umenewu. Zowona mufuna anthu ammaboma ena aziwona ngati ku Lilongwe kulibe madona abwino eti? Ngati munawona kuti kunalibe akazi abwino osasiya bwanji mudikire zibwenzi zanthu zitsekere sukulu mma university apamwambawa bwanji? shupiti tipanditsatokha wina. Kalekale olo akamati miss malawi zinkamveka kuli achina elizabeth pulu osati mwayamba kuchitazi.
chinyengo basi,masaya ake amenewa nkukhala miss LL?amayenera kukhala MR LL…..
Beautiful!!!
Frankly, the only problem I see in this young lady is that she has poor teeth alignment. Other than that, she has all it takes to be an African queen.
My girlfriend is far much beautiful than! !!!!!!!!!!
miss lilongwe indeed
the worse has happen
Koma ku university imeneyi mukumanamizana miss Lilongwe? dimvetsa ngati anayankha bwino mafunso osati kukongola. pali nchani pamenepa
Koma ku university imeneyi mukumanamizana miss Lilongwe? kulibe akazi kumeneko ndithu. Ndimvetsa ngati anayankha bwino mafunso osati kukongola. pali nchani pamenepa
Hokoyo!
Please forgive the judges. They were only doing their job. Out of all the ugly girls that were paraded on the catwalk, Leticia was the most beautiful!