Email a copy of 'Lilongwe City to allow media coverage during councillors meetings' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lilongwe City to allow media coverage during councillors meetings' to a friend
We, Centre for Human Rights and Rehabilitation and Centre for Development of People, have learnt with great shock the devastation...
Town Yathu yopanda malamulo….ndichifukwa chake achina oyimba awa amawagwira ku Dubai…Unve ochoka nawo ku Malawi… Kuti town ikhale bwino….you need to be aggressive..as aresult mudzawona kuti Lilongwe ingakhale town..yolemera kwambiri…pliz separate city activities ndi ndale…..who is a vendor kuti atisowetse mtendere…
Vero,
A vendor is a Mayor by definition. A vendor has taken over the city in the deafening absence of substantive His Worship the Mayor.
I didn’t know we have a Mayor in Lilongwe. Where has he been all these past 8 months? Anyway better late yhan never.
good idea tizimva mmene muziyankhulira mbwerera ngati ku parliament zopusa ayi mwamva
Bwana wa nkulu umandiwaza………. No shaken
Koma yesesani ukhondo mtauni mu anthu zoona mizimbe kaya china chili chonse kumangotaya penapaliponse zoona. Aphuzinseni ukhondo Anthuwa umve wachuluka.
zikusokoneza town Yathu ndi ndale…….if we can separate ndale activities ndi city activities…..zonse ndi zotheka….