Email a copy of 'Lilongwe Mayor faces crisis of confidence from councillors' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lilongwe Mayor faces crisis of confidence from councillors' to a friend
Councillors in Malawi’s northern border district of Karonga together with chiefs and Members of Parliament have stop attending government meetings...
Mayor wa DPP angapange chitukuko chowoneka, anthu a Nac-gate ngati amenewa.
Voti ya Umayor ma Councallor munasakha bwanji?
But guys the mayor is too old no wonder he is very passive iye Bola wadya, ku pita ku toilet. Ndi kugona kwa iye wamaliza masewero. Komanso no wonder he is dpp watengera tulo Ta apm. Nonsenu just resign apm ndi mayor okalambayu
Stupid old mayor u are very stupid
Just resign ulibe mzeru we need anyamata ngati noel chalamanda othamanga ndi chitukuko
Achoke otherwise we will go nowhere! Is he well exposed? I doubt it!
Akulu, osangoti munali a federation ndikale bwanji. Nanga magetsi ndi federation zikugwirizana apa?
ha ha anthu musatisekese Mayor akukanika ntchito? Kodi makhansalawo ntchito yawo ndi mayesa ndikuthandizana ndi Mayor Muleke ndale muyambe kutukula Lilongwe agalu inu
kukalamba ndi ntchitoyi sidzikugwirizana we need munthu wachinyamata to help us. lilongwe is the capital city koma eeeish kwaipa bola panakakhala opanda ma councelors the vendors r back in the streets nde kaya ndi politics kaya
Ndatopanaye ameneo nkunyumba kwake ngwaumve uyu iyaaaaah
I think it’s fair t compare current and previous mayors of LL NOT wth another city bcoz they have different sources and magnitude of incomes. Even salaries of employees and offices & machinery are different. That shows how richer is BT. city than LL city.