Email a copy of 'Lucius Banda snubs UDF move to DPP benches' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lucius Banda snubs UDF move to DPP benches' to a friend
As Malawi is still remembering a teen girl who was brutally murdered by her cousin and had her private parts...
all politicians are one. All are business people they just want kukolola pomwe sadalime.
kuganiza mozama kumeneko achikulire
No different UDF and DPP there all rubbish
That’s what happens when one feels is too big for the Party.
Lucius Banda nakuona una mahala nadi ntchindi zikumwenelerani bwana Soldier wabakavu. Kanthu ako tiye navyo.
Bwana Lucius Banda, You have showed the maturity in politics, osamangotsata zilizonse, even zolakwika kumangowombera mmanja, a phungu enawo awonetsa kufooka, pa chichewa timati ndi a kwalimbauta, komanso UDF ndi ya ku banja kwa muluzi, ndikovuta kutsutsana ndi banjali, kumbukiran a Sam Mpasu ndi a Friday Jumbe, a Bandawa atha kuwachotsa mchipanichi. Chipanichi Chili Ngati Momwe Chilili Cha DPP, Zipani za kubanja, palibe angatsutse zomwe akubanja kwa munthalika akufuna.
Ku Malawi kukadakhala ma MP ozindikira ngati Lucious Banda, bwenzi Malawi
atatukuka zedi. Pitiliza kuchita zomwe anthu akutuma osati zomwe chipani chakutuma.
Lucious you are a Superman!!!!
Bravo Lucious Banda! You are a Superman!
We love you!
Ameneyo ndiye serious osati Lucious
Thumbs up for Soldier, do not allow to be used by Atupele whose political muscle has been usurped by greed. Now I agree with what one politician said that Atupele is a kindergarten suckling baby.