Email a copy of 'Lucius Banda’s song promoting girls education in Malawi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lucius Banda’s song promoting girls education in Malawi' to a friend
The country’s consumer and human rights activist, John Kapito has taken a swipe at Blantyre Water Board (BWB) for its...
Lucius anali kale, pano akungoyankhula zankutu zokhazokha. Tionana 2019.
Tatulutsani chimbale cha Ulamuliro wa APM so far.
mbuzi g imeneyi
Wawa angoni ndakunyadilani mr banda inu ndi mzathi wathu basi wina afune or asafune u will remain the soldier of the power ndinu
This is excellent and fabulous
big up lucius big up sawako thats tha way 2go
Tikungomva mukunyoza Lucius,walakwitsa chani?mtima wansanje amalawi suzatipitsa kulikose,monga mukuganiza kuti inuyo mutati musagule nyimbo ya Hon Banda,nkulu ameneyo family yake igona ndi njala?Komaso kukuona ukutukwanawe uli mbuuu!!!! Ulibe chirichonse ngati ine nemwe.Muchedwa osamalimbana ndi awo zawo zinaera kalekale,koma ngati muli ndikuthekera kwanu,pangani zanuzo dziko likudziweni kuti ndinu akutha kuposa Hon LUCIUS CHICCO CHIDAMPAMBA MWANAWAM’MUDZI BANDA
Lucius, this is better for the nation and our God than talking political pleasing.
Adali kale kape ameneyi, azigula ndi Achawa nyimbo zakozo wanva?
Our next president.