Email a copy of 'Lucius hail Prophet Bushiri for charity: Piksy remains ‘hater’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lucius hail Prophet Bushiri for charity: Piksy remains ‘hater’' to a friend
Silver Strikers supporters have accused the club’s board of directors of breaching the club’s constitution by resolving that there should...
Tingogwiritsa mawu not kuw€luzana, inu mumafuna kuti akhal€ wosawuka Bushiri or mukufuna uthnga….. No kritiks mw€€ yowoyani vamahala
paja malemba amati ndintchito zawo tizawaziwa inde gwiritsani YEHOVA MULUNGU yekha osasata chuma akuza msanga Yesu kutenga aketu tilimbike kuyimapatanthwe lija tanthwe ndilo khristuyo ngati tipirira tizankako kuli chuma chosathako.
Mulungu wayandikiradi
Kaya
piksy and uwa folowers u dnt knw we dnt knw and they dnt knw so why ur critsing a man of jah let him preach and enjoy u sing u want wat nt money u pipo ur blind
Mukuzaona kut mitundu ikuwukirana nkhondo njala komaso aneneri onyenga muzaziwe kut nthawi yayandika
Mulindi Soka inu anthu a chuma poti zanu mukudyeratu…. ndichapafupi ngamila kudutsa pa m’bowo wa zingano kuyerekeza wachuma mkovuta kuti akalowe ufumu wakumwamba… ndipo adati kwa iye ”ngati mundigwadira ine nachita mchifuniro changa ndidzakupatsani mtendere wadziko lino poti zonse zinaperekedwa kwa ine ndipo ndimapereka kwamene ndamufuna…” ndipo iye adati ”kwalembedwa kuti alipo mmodzi oyenera kupembezedwa ndikuchita mchifuniro chake ndiye MULUNGU Mfumu Yachirengedwe Chonse… Olitsata Bible akumva ndipo sangakanire… big up Piksy anthuwa ndamodzi…
Muli ndi soka inu anthu achuma poti zanu mukudyeratu Pompano. Ndichapafupi ngamira kudutsa pa m’bowo wasingano koma sichapafupi kuti wachuma akalowe ufumu wakumwamba. ndipo satana adati mchipululu muja ”ngati mundigwadira ine ndikuchita mchifunira changa ndizakupatsani ine mtendere wa dziko la pansi, poti zonse pansi pano zinaperekedwa kwa ine ndipo ndimampasa yemwe ndamufuna.” ndipo iye anayakha nati ” kwalembedwa kuti palibe oyenera kupembezedwa ndikuchita mchifuniro chake koma MULUNGU Yekha Mfumu Ya Chilengedwe chonse…. Yemwe amalitsata bible akumva ndipo sangakani… Piksy big up asakupusise anthuwa ndamodzi…
You people who say Bushiri always preaches about wealth or riches thats a blue lie. Bushiri extremly good at preaching. he one of a few prophets who know how to teach word of God. If you like go to his church and see..
no power to judge lets just leave it in the hands of the most high our Lord,He is the one to judge wheither ths is true ministry or not