Email a copy of 'Lutepo exaggerating illness , fit to stand Malawi cashgate trial -doctors' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lutepo exaggerating illness , fit to stand Malawi cashgate trial -doctors' to a friend
Ahead of the main event in September, the Lake of Stars (LoS) will be holding events in Mzuzu and Lilongwe...
Jxt give us our money baxi
koma nkhani imeneyi izatha? Tatopa nkudikira!
Nkhani ikikoma iyi oswald suspect oswald lawyer what a coincidence malawi woyeee
Ukunamizira Kupenga,upenga Zenzeni.Yalakwa Yalakwa Kayankheni Milandu Lero Wankaka Wasanduka Wa Acid. Try God Che Lutepo
Follow his trail: he started getting “sick” soon after making his zodiak statements. He first hid and then made the “revelations” which led to our own Nankhumwa to come up with “cctv” hallucinations! Follow!
Ndie kusadzakhaleso ad jan tiziiwale izi mugamulen basi 21 yez minmum
WANA WATHU aKUPHEDWA ku joni uko
Ndalama zoti tikanawalembera ntchito kuno kwathu munaba
Ndinu
Mukungu akuwona zonzenso
Very interesting!!! So you mean in the whole cash gate saga no Mmwenye is mentioned??? Zodabwitsa kwambiri!! Komatu alipo in the likes of Karim of Lido/gratolite, Kamarat of Shayyan in Blantyre and Amad of Ocean Industries in Lilongwe.
Amai JB please bwelani muzamuthandizeni mwanayu. zamukulira sakuziwa kuti agatani pa mulandu umenewu. paja nthawi ija mumati mwananga wanga Lutepo. Lero mwana wanu uja zamufika mukhosi. Mai please bwerakoni munthu uyu akusowa back -up monga iye anachitira nthawi imeneija kwa inu
Apa pamene paonekele u idiot wa malawians. How can some one be fooling the whole country visiru va Boma they are using him on expence of poor malawian abweze kaye ndalama zo.