Email a copy of 'Lutepo faking it, marginally remorseful - Court' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lutepo faking it, marginally remorseful - Court' to a friend
Police in the Malawi northern border district, Karonga, Tuesday rescued the two suspects of albino abductions from an angry mob....
shame be on all cashgaters Mal onawi is suffering because of you. may GOD bless u
Zovuta kumvetsa2 wawa
Who arrested Lutepo is it APM or JB? I think some people don’t follow issues
Ndalama za boma ndi za tonse a Malawi. Nde tikukupemphani kuti mufufuzenso ku PVHO amatulutsa ndalama thru Stecelia Motors wa kwa che mussa. Timaona zonsezi. KUmanamizila kukonza magalimoto and yet PVHO has its educated mechanics who can do it all. Fufuzani ife tikuona zonsezi.
The wicked shall perish let Lutepo rotten. The judge is right.
zachisoni
IWE KAYA UKUTI NDIWE ” THAKO LA MMWENYE”
WANBVA KUTI NKHANI IMENEYI? KUNGOKALIRA MISECHE BASI M’MALO MOTI ULIMBIKIRE KUGWIRA NTCHITO JAMANI
kodi inu a ACB chifukwa chiani Alexander Makina mpongozi wawo wa a lipenga a kumangochi kuno sakumangidwa? komanso chifukwa chiani munatumiza mbava ngati imeneyi ku embassy?
tikumva kuti anagula nyumba zambiri mu lilongwemu komanso wagula estate ndi ndalama zokuba.
Chonde chitanipo kanthu apa a matemba
This judge is very intelligent. Indeed Lutepo is marginally remorseful. If Joyce Banda won the 2014 elections, do you think anyone would have touched Lutepo. God is in Control in all this!!!!!!!!!!!!!!!
Nayeni Lutepo ameneyo, osamusiya kapena kumumvera chisoni ayi! Adaphetsa ndipo akuphetsabe anthu osalakwa muno m’Malawi. Alandire mphotho ya kulakwa kwake ameneyu.