Email a copy of 'Lutepo gets 11 years jail for Malawi cashgate' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lutepo gets 11 years jail for Malawi cashgate' to a friend
Supporters of the Democratic Progressive Party (DPP) and it's political partner the United Democratic front (UDF ) on Thursday engaged...
11yrs zachepa chifukwa wapha miyoyo ya abale athu kamba kosowa mankhwala mzipatala akanakhala moyo wake wonse.
NGATI BOMA LILI SERIOUS ZOTHETSA KATANGALE MUDZIKO MUNO NTHAWI YAKWANA KUTI BOMA LILAMULE A ACB KUTI AYAMBE KUFUFUZA ANTHU AMBIRI AMENE AMANGA MANYUMBA AWO MUMA NEW SITE MU LILONGWE KUTI NDALAMAZO ANAZIPEZA BWANJI COZ AMBIRI MWAIWO NDIMA CIVIL SFRVANT NDIMA FAKE CONTRACTORS. Apo biii cashgate siidzatha.
Asala anzakeo
Zaka 11 ndizokwana koma 1.7b zili pati?
apatu ife tiwotcha ndende za dziko muno amangeso okhaokha mbava za dpp kaye anthu anji mukumanga anthu olakwa kumene akale ayi we are not happy with this onse ofuna mademonstration plz plz imbani ku
Wakula watha ukamacheza ndi mbava ndi choncho chobwera chimakhala cha nonse whether you do with them or NOT
Zayambapo onse omwe anaba alowe basi osawanyengerera
Good! This shows that Professor Peter Mutharika is good and a democratic,DPP woyee!
Akulu akulu kawirikawiri tisamayankhule kapena kunyadira kwambiri nzanthu akaona mabvuto ngati awa ifenso ndi anthu ngati m’bale wathuyu,Chaonatu nzako chapita mmawa chili kwa iwe,ndipotu moto akuti umayaka komwe kwasala tchire,muzifunse kuti ngati mumalakalaka kupeza mwawi wokabwereka nawo ndalama mmabungemu komanso osafuna kapena kulepheranso kubwenza,ndiye mwawi ngati umenewu ukanakupezani simukadalola inu? Ndiye amene sadachimwepo ayambe kumugenda mwala uyu!
Imagine a scary state machinery like Dausi, Masangwi, Ngalande and president approach you to use your company to steal govt money. It would take the presence of the Holy spirit to give you courage to say NO. This was the same with Lutepo and other cashgate suspects who were approached by PP machinery and senior civil servants to steal govt money. Ukakana siuphedwa poopa kuti ungaulule? Ngati company zako zili ngati za Lutepo zodalira macontract a boma ma contract suwaonanso zikatere. Imagine how big company like Mullie suffered under PP nde kulili afinye kampani xing’onozing’onozi? z