Email a copy of 'Lutepo’s wife, daughter risk arrest: DPP asks cashgate chief suspect to seal ‘deal’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lutepo’s wife, daughter risk arrest: DPP asks cashgate chief suspect to seal ‘deal’' to a friend
Former leader of the Malawi Congress Party (MCP) John Tembo and Monsignor Boniface Tamani joined the federalism debate this past...
Chuma chapadziko chodwedwa ndi njenjete..Koma kumwambako kudzala ntchito Kaya ndangodutsamo ine.
koma abale inu kumadyerera ife kumasauka mulungu akukhululukireni
anyanya
Kkkkkkk kkkkkkk JB is afraid of Lootepo. She knows that she is in water.
When a legal officer wants to ends like curtains they join the government which doesnot win cases
Mukuyenera kuchita khanthu mwachangu!
Nanga Mserembo anakatenanga chi thumba chama hundreds of million Kwa Lutepo through lawyers joe and max?
Abale, ndawerenga ma comment onse koma tiyeni tisamale. Vuto pa Malawi ndi umphawi ndipo ndi umphawi omwewu umene anthu akuba ndalama za boma amabweretsera ziphuphu komanso ngakhale kugula olemba nkhani kuti asokoneze a Malawi. KODI MUDZIWA BWANJI KUTI MUNTHU WALEMBA NKHANIYU WAGULIDWA NDI LUTEPE OLO LOYA WINA KUTI APEZE SYMPATHY KWA ANTHU NDIPONSO AKUSOKEONEZENI MITU. ABALE PA MALAWI NDI NDALAMA CHILI CHONSE CHINGATHE KUTHEKA, TIYENI TISAMALE NDI NKHANIZI.
Why force Lutepo to implicate JB? Witch hunting eti? What if she is innocent, will she still be implicated for the sake of Lutepo’s freedom? Say the truth and truth shall set you free!
Kodi osamukwenya Lutepoyo kuti aulule amene amamutuma? Zinazinso ndiye bola milandu ngati imeneyi aziweluza mafumu. Mpaka boma likusowa poyambira?