Email a copy of 'Machinga hospitals run out of malaria drug, LA' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Machinga hospitals run out of malaria drug, LA' to a friend
Despite bold steps taken by various stakeholders in reducing cases of child and forced marriages Ntcheu district is registering increased...
Very pathetic indeed
Please,catch these thieves and over dose them with the same medications!!!!
Atupele Muluzi akusowa LA kikiki abiti Chanil akusowa LA kikiki abiti Annie apita pamsika kukagura LA kikikiki
a Malawi apapa amene ali ndi info please put it on Internet. Atchuleni mayina awo. That is the only way to expose them. Kaya ndikumpoto, ku mwela Pakati atchuleni mayina awo. TATOPA NAWO AKUBAWO. DZINJA LIKUBWELA NDIYETU AFA AMBILI
The people responsible for the drugs are stealing. Amalawi tilibe conscious kodi? Mulungu akukuonani nonse mukuba ndipo simifika patali. Azibale anthu asamavutike chonchi
Iwe Chilikumtima kabwenze mankhwala ndisanakuulule. Tikukuonanitu!
UDF Ili mmboma kwawo kumeneko ayisova. Nanga phindu lokhala ndi olamula mlimenero
nde dausi akutani if spies cannot help resolve these mysteries. failed state indeed!
Mchipatala mulibe mankhwala koma mutapita paka grocery kapafupi ndichipatalacho kupeza kuti akugulitsa mankhwalawo ndiye kuti akulu achipatala akudya momwemo
Don’t blame cashgate on the shortage of drugs, this is because of some stupid ideotic fools who steal the drugs, very sad. Just know it shall never be well with you.