Email a copy of 'Malawi albinos call for divine intervention on increasing abductions, killings' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi albinos call for divine intervention on increasing abductions, killings' to a friend
Glamour, glitz and better describes the 2016 Malawi Achievers Awards, improving every year since their inception. This time held outside...
this z total inhuman, blame game cant work, pliz malawians lets come 2gether & STOP killing our brothers. sisters or children. Informers, community police & volunteers policing of all ages should be introduced and empowered n all constuences, all pple practicing traditional healing should be registered under one orgnisation, regulate them, since they r major contributors to albino abductions, Gvt should properly Research, Plan & Develop to extinqish this demonic actions once & for all.
This country’s leadership is satanic that is why satan is having a free ride. The activities of the citizens mirrors the kind of leadership we have. This could not happen during Kamuzu’s time. The best way is to change the leadership in 2019.
Apa akagwidwa kumangopha basi zaonjeza mpaka kupha mwana wa zaka ziwili ndipo anthu aku nsanje munachita bwino kuotcha anthu seven aja keep it up asena tiyeni tose amalawi tikagwira anthu amenewa tiotche wapolice akafuna kuwateteza aotchedweso
Fiti ndi fiti.chilamulo Chotete wakupha nchabwino wako okondedwa asanaphedwepo.azanga mulinawo abale anu a albino chenjeran.poteteza ndi kudziteteza,zigawengazi tizikonze bwinobwino monga mudziwa lamulo lasatana liteteza satana.chenjera!!!!!
Stupid government,stupid president,stupid police who always just follow what the law entails not justice,stupid the fucking law which says witchcraft never exist ndiye anthuwo ziwalozo akumapita nazo kut?Sinthan lamulo limeneli ngat mukufuna kut anthu aziulura za ufiti zimene masing’angawa akuchita ndi ziwalo zimenez.Ine sindiulura pano ndikuopa angakandisumire kut ndamutchula kut ndi mfiti.Oh!Ndinaiwala another stupidity should go to all secular humanism staff.
Right approach, this time. The devil is the one doing it. Komabe aboma apereke security yokwanira kwa abale athu with albinism. Asasowe ndalama. Ena chifukwa chaumphawi akumakaphedwera kochita timageni olo kumunda. Pomwe ana asukulu akumaphedwa chifukwa chopita masukulu wambawa opanda chitetezo. Bwanji inu aboma muwapezere masukulu abwino ana amenewa nkumawalipilira nkumawateteza? Izinso ndizovuta? Atetezeni abale athu amenewa, osangowopseza mpakamwa kuti mudzawalanga ngati kuti ndinu amene mumaweruza milandu. Kumakhothi kuli anthu ena. Kupolisi nako kuli anthu ena. Actions speak louder than words.
Disturbing behaviour of certain pple who continue killing innocent souls like that.
May the Soul of the innocent child rest in peace and May God help our Country to be free from this danger. Amen
BEYOND HUMANISM