A Prophet/abusa che Isaac mulibwanji? Tingoyerekeza mene mwavaliramu muli ku pulpit kudyetsa uthenga wa Ambuye. =palibe amene anganene kuti amen.
Pepanitu pepa
chakanika
9 years ago
koma uja akumasoskosa uja ndi kagulu kake akuti mulanje mountain ndi ya alomwe uja analiko? kaya zimenezi akuti nazo bwanji ndi u MP wa fake?but all in all congratulations un
wawaruh
9 years ago
keep it up zex and ja,u r the best among the best .
talibo
9 years ago
I’m the road ndiyemwe yemweyi viiiiiiiiiiiiiiiiiii zalewa, kenakono chirekano airport. Ukataika kuno sikwanu! Izeki ndi jacob anyamata odyera pakamwa.
A Prophet/abusa che Isaac mulibwanji? Tingoyerekeza mene mwavaliramu muli ku pulpit kudyetsa uthenga wa Ambuye. =palibe amene anganene kuti amen.
Pepanitu pepa
koma uja akumasoskosa uja ndi kagulu kake akuti mulanje mountain ndi ya alomwe uja analiko? kaya zimenezi akuti nazo bwanji ndi u MP wa fake?but all in all congratulations un
keep it up zex and ja,u r the best among the best .
I’m the road ndiyemwe yemweyi viiiiiiiiiiiiiiiiiii zalewa, kenakono chirekano airport. Ukataika kuno sikwanu! Izeki ndi jacob anyamata odyera pakamwa.
Amaopa mashingozi
Aaaaah awaso awaa Aaaaah! zomwezitu a Izek. Un coordinator meeting a mfumu. Akumvana anthuwa? pa malawi tiyeni nazo