Bambo ngati anali ku Army banja lonse limathera ku army chomwecho ndi kupolisi.Umadabwa tina tatifupi ngati ndondocha tili ku army ndi ku polisi.Tinalowa bwanji timeneti?Katangale basi.Merit imavutirapo kuti zinthu zambiri ku Malawi.No wonder output ya zinthu zambiri imakhala substandard.
wellie
9 years ago
The problem is that MDF is the one in the fore front promoting shortcutd when recruiting soldiers the army is full of officers children for an ordinally person’s son or daughter to be recruited is not easy unless u are well connected to the high ranking officers so osamatipepeletsa apa
NDI BWINO KU MALEMBA NKHANI ZO THANDIZA KU MTUNDU WA AMALAWI
muhawi
9 years ago
The bribery behavior that take place during recruitment has led to this. these are the very same officers that are used to doing this that are hungry for money
Bvuto timasogaza mitengo kusiya mulungu ask msogoleli mlomwe pa nambala iyi………… ndikuuzeni za mankwala a ntchito.
Awali mustafa
9 years ago
Mwayi kuti kuno kulibe nkhondo bwenzi ena mtundu wakwawo onse utatha nsankho basi muzaziona dikirani
McSpiceKay
9 years ago
i cn’t w8 4 intek 2 b held!
Mapuyamurupare
9 years ago
Mbola zenizeni. Something fishy within the army (MDF). Side effects of Cashgate at work now. Ngati army ikulephera kuwagwira anthu amenewa ndiyekuti chitetezo palibe pa Malawi. With a very good army tikamva kuti uje ndi uje agwidwa. Army is getting paid for NOTHING. No intelligence I guess. A Community Police ife tikhoza kuwagwira akubawo. Tikadagwiritsa nchito anthu amene alipira ndalama kuti alembedwewo popeza amene walandira ndalama. Apasilana kuti ndalamazo? Nthawi yanji? Alembana nchito kuti ndipo liti? Popeleka ndalama mboni idali ndani? Komanso opeleka ndalamayo amangidwe / akalowe chifukwa ndiwa corruption / ziphuphu. Ngati amaimbirana ma foni amagiritsa ntchito number yanji… Read more »
Paul Yorkey Longwe
9 years ago
Gvt must b transparent & equal interms of job opportunity not discriminating their tribes thus y many pple r indulgung in theifting

First mangani odandaulayo.