Email a copy of 'Malawi army soldiers kill 2 over Dzalanyama' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

64 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Baba
Baba
8 years ago

Ntchito Ya Asilikali Ndi Imeneyo. Palibe Chodabwitsa Apa.Ngati Mukufuna Mtendere Itanani Apolisi Asilikali Achoke. Failing Which Anthu Apitirira Kuphedwa Ma Soldier Samachita Chibwana.

DR TONDE
DR TONDE
8 years ago

Zodiac broadcasting station is a stupid radio station that i have now stopped listening to now. No moral responsibility whatsoever. You know they put this story as its weekend feature story! For what! Nyasatumes.don’t join stupid zbs

chipwilikiti
chipwilikiti
8 years ago

Comment 40, 12 and 6 i agree with you guys, the army are not above the law afterall iwowo akalanda makalawo kapena mitengoyo what do they do with them . A kansala take the matter up, find out why mitengo yachilengedwe yodula koopsa imene analanda a MDF yasowa ku MDF heaquarters komweko after Commander wolamulira asilikali olanda makala, mitengo ndi kupha anthu atalamula kuti mitengo isamalondeledwe cholinga choti abe akagulitse for millions of money. A president chonde pakhale commission of inquiry into the death of these two. the other thing is we wonder why now these soldiers are killing civilians… Read more »

jk
jk
8 years ago

MALAWI FEEL SORRY FOR YOURSELF LOOSING A LIFE IS NT A JOKE

Harawa
Harawa
8 years ago

Akuchita bwino a army kuteteza nkhalango ndipo amakala awa amakhala ndi zida zoopsa ndipo izi ndi zina zomwe zimawonjezera mkhwiyo mwa army athu.

Long Live Malawi Defence Force, Long Live Malawi.

Simbi
Simbi
8 years ago

Killing defenceless people. Is this the sign of might on the so called MDF? Imagine killing an 80 old granny. Do we really have sensible soldiers that a country can be proud of? Whoever is applauding the behaviour of these useless so called soldiers should be ashamed of his/herself.

ndatopa
ndatopa
8 years ago

Zoona zake ndizoti Boma lipeze njira yoti aliyetse wa kumudzi olo wamtauni asamaphikire makala basi. Nchenjezo ndiloti army ngati mukuphadi anthuwo siyani chifukwa Mulungu sakondwera ndizophana ayi. ngati mwaphadi pemphani chikhululukiro kwa mulungu akukhululukireni basi. ziwani kuti umphawi ndiumene kukupangitsa zonsezi kuti anthu aziwotcha makala kuti apeze chakudya chalero.

Mathanyula
Mathanyula
8 years ago

pathako panu amene mukuti a Army KUCHITA BWINO MCHITIDWEU…..Once again pankholo panu….. kuchokera pa Kampepuza, Msipe, Balaka market, Chingeni, Manjawira, Senzani, Chitale, Phalula, Kanono, Kamwamba kuzafika Zalewa malo onsewa munali nkhalango koma mitengo anamliza…..mwano wake nkumachita kuyala makala mbali mwa nseu. bwanj ngati muli oteteza osabwera malo amenewa kuzapha anthuwa? Ndakwiya nanu

malawi
malawi
8 years ago

MUKAONE THUMA FOREST ANAMALIZA KUMENEKU MUPITENSO ARMY

Mbuya
Mbuya
8 years ago

If that is true God is watching u repent ur sins

Read previous post:
Police launch special operation to net Blantyre murderers

Malawi police in Blantyre have launched a special operation to hunt down murderers that have killed some people in the...

Close