Email a copy of 'Malawi banks warn each other on Kaonga, Nserebo 'loan tricks'' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

41 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
marika
marika
8 years ago

maranatha ndi school ya ukape ndi yakuba, ngakhale ana amawabera ngakhale ma cell phone ndi masuitcase a zovala chifukwa cha umphawi. Alibe ndalama awa komanso amangolemba unprofessional administrators. Headmaster alibe say ku maranatha. Azipunzitsi ndiye kananja. Anakwatira ka mwanapiye akawongawa. Kodi munamulekeranji chiphadzuwa uja? Kodi mumangoyamba ma business mulibe ndalama? Nkhanza mumachita pomabweza ana atalipirako half school fees zija kani inunso mumalephera kulipira ngongole? Shame on Maranatha.

GRM
GRM
8 years ago

Are banks becoming a cartel? Stupid banks they refused me a pay day loan of 500,000 nkumati it is equal to my salary Ali nditenge 250,000 yet I was to give all the money once I receive my salary. This guys are crooked. Now they are crying louder coz akumana nawo mbava zinzawo. Stupid banks

MGULU
MGULU
8 years ago

SPECTATOR WALASA, AFTERALL MULI BROTHERS BAND USED SAME TRICKS FOR HIS COMPESATION(S)!! NOW MNGULU WINA AMUCHENJERESA APA!!!

NTHAWI ZINANSO TIZIFUFUZA BWINO, NTHAWI ZINA A DEFENCE AMATHA KUYIKA DALA WEAK DEFENSE ILI PLAN.

Fatso
Fatso
8 years ago

Akhaulitseni ma bank onse.More fire.If i remember well ma bank akhala akukana ma credit bureau.Iam sure zimenezi akanawauza a bureauwo ngati mmene achitira kuno ku RSA!Kaonga tiye naye Mpinganjira waba MSB.

Kondwani
Kondwani
8 years ago

Gulugunya U Can’t Attack The Whole Innocent Tribe. Ndiwe Chindere Tikurowenge.

gulugunya
gulugunya
8 years ago

Kaonga is professional thief. K785 million kwacha is just too much for Malawian bank. The Kaonga is Mtumbuka and the judge who handled the case is also Mtumbuka. I smell a dog here if not a rat. Another Tumbuka is up again for compensation over trivia matters. Tumbukas are thieves. The other tribes watch out with Tumbukas. Mark my texts.

Najere Chitekwe Gelevulo
Najere Chitekwe Gelevulo
8 years ago

Kubera bank…..no crime. Atibera kokwanira. FDH ndimatemberero chifukwa chogula bank ya MSB amalawi akulira, iwo nkumasangalala. Inenso I am suing you for K1bn. Cashier wanu sanandipatse moni lero

spectator
spectator
8 years ago

Wakuba akabeledwa amapenga heavy. Palibenso amene amanva kuwawa ngati wakuba akabeledwa.

Diwa
Diwa
8 years ago

Za chamba imeneyo nde bank kapena finca, unprofessional ma bank a m briefcase.

parice
parice
8 years ago

bwana james stop confusing malawians, how can one use tricks to obtain a loan from banks,ngati ma bank akupangidwa zimenezi then dey shud blame themselves for poor security,osangoti kungodzuka uko kuzaononga cv yanzanu,those pple they work day n night to rich where they are,work hard the success will follow u,siyani majerasio.

Read previous post:
Malawi ‘student support’ group formed to curb drop out at universities

A group called ‘Student Support’ has been formed to raise funds for underprivileged students who fail to pay their tuition...

Close