Email a copy of 'Malawi civil servants' pay rises: 45 percent' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

122 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Gift Ndhlovu
Gift Ndhlovu
9 years ago

Timuyitane mwiniwake azititsogolera,kunjako nzimene mukukatengako?anzanutu sakumapanga tikuzionazi.

Chimtuwitsa
9 years ago

Ichi mchifukwa chake malawi is the poorest countries on the land. Akuti if they accept the 50% our economy will collapse yet million of kwachas is going into these greedy leaders. It is only gods kingdom that will bring good and perfect governance.

Kondwani ndinu
Kondwani ndinu
9 years ago

Dzikoli likufuka munthu olamulira wachifundo oganizira anthu osauka apo bii waku jon basi kuthawa mbava zoyendetsa dziko

tom alexannder
tom alexannder
9 years ago

remember to pay arrears for teachers who were promoted to PT2 in 2011

tom alexannder
tom alexannder
9 years ago

remember to pay arrears for teachers who were promoted to PT2 IN 2011.THE INCREMENT IS ATLEAST FAIR , GUD FOR A START

Steve Binda
Steve Binda
9 years ago

Kodi grade L yomwe pali aphunzitsi ambiri no increament? Your reply is highly needed.

Do or die
Do or die
9 years ago

Mphawi sazatukukabe mpana kale. Muzimvabe kukoma ndi inu nomwe akumipando yonona inu

Ine ndemwe
Ine ndemwe
9 years ago

Chomwe sindikumvets ndichomati kuyambira pa 1 October, kodi finacial year yayamba kumayambira October? Mesa hike ili consistent ndi new budget? Nde July- September zili mu chaka chiti?

paul
paul
9 years ago

ikufunika apa ndi harmonization, osati zimenezi

Mike
Mike
9 years ago

Increment yokomera akumipando okhaokha iyi. Meaning to say amphawife tizingosaukabe kugwira ntchito ngati ykugwira ganyu.

Read previous post:
UDF, DPP in ‘governing pact’ not a coalition –expert

University of Malawi political analyst Dr Henry Chingaipe has said Democratic Progressive Party (DPP) and w United Democratic Front (UDF...

Close