Email a copy of 'Malawi College of Accountancy lecturer arrested over cashgate' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi College of Accountancy lecturer arrested over cashgate' to a friend
Campaign for Female Education (Camfed) in Malawi has indicated that although various organizations were coming up with interventions to help...
ife tinathawa umphawi pano tili ku theba kugwira ntchito zomwe zikadatukula lathu dziko. kuzunzika. abale athu kumalawiko kumudziko tikufunako koma mantha atigwira ndizomwe zikunvekazi……… tidzingogwirabe ukayidiwu kuno.
Kodi azingomangidwa osalandidwa kena kake?? ali ndi chuma chambiri chooneka osatengako manyumba ndi ma house ooneka wa bwanji??? mcheew imandikweza dpp bwanji nkhani imeneyi kunali kungoauza apange surrender chumacho coz olo akasekeredwe 20years azidyabe money yakubayitu
muchimina
Why don’t you arrest Radison Mwadiwa- Former Secretary to the Treasury. Newby Kumwembe, Dalitso Kabambe, Charled Tchuka etc.
Nanga JOICE mummanga liti? Mukumamuwopa akafufuma.
don’t waste our time reading fake stories.kumangomanga anthu chifukwa chowawonerera. akuba eni eniwo mukuwawopa. za zii.
kodi inu a ACB mpongozi wawo wa a Lipenga aku mangochi kuno Alexander Makina yemwenso makolo ake amakhala konkuno, mfana oyipa wakuba bad mummanga liti. Poti iye ndi amene anali conduit pakati pa mphwiyo ndi amayi. kapenatu ingokhala mob justice- zimatiwawatu ife mafana amene aja akamanjoya ndi dollar yokuba ndikumaoneka ngati a mzeru heavy.
The fear I have is that the more Mphwiyo is pushed to the ground the more the top big guns will be apprehended. kwendenayo!!!!!!
So, why are your afraid? Are you one of them?
Mulopwana ndiwe galu. Ufa ndi umphawi.kadzidzi wachabechabe iwe.
wina aliyense ndimbava ku Malawi