Email a copy of 'Malawi coughs millions for Mutharika shoe shiner, hangers-on allowances in New York' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi coughs millions for Mutharika shoe shiner, hangers-on allowances in New York' to a friend
One the country's mobile service providers, TNM, has given tricycles to three more winners in the Tikolore promotion, which aims...
Chaona ine nsanje a Malawi…akanapita wanu wachiale sibwezi mukudandaula zonsezi…..asiyeni anthuwa agwire nthito tidawapatsa tsiku lovota lija!!!!
Haters ,sign of poverty
Zitafuneni ndalamazo tiyeni nazoni. Tinakuvoterani dala ndie lero tisadandaulenso ai. Ndipo amene akudandaulawa amangeni ma key a hand caff zao mukaponye munyanja la lake Chirwa kakakakakaka.
His wife us there. Adzipukuta nsapato. That’s part of her duties.
Ugly betties!kuno ndi kunjatu muziziwa anthu akukudandaulani.
Mavuto alipo. Mpaka na wopukuta nsapato ndi wokolopa nkhope ya a mayi (shoe shinner and first lay face make up).
ZOVUTA: ukuti APM ndiwonyasa nkhope? Iwe bambo ako okongola nkhopewo bwanji sanakhale president. Palibe ungapange ndimakudziwatu
eh Malawians.dont u get tired.thngz are being messed up by lower level offcals,DC,DEMs.DHO,but u dnt say anytng.
Stupid Malawians!Only good at talking but no action.Action speaks louder than words.Nchifukwa chake amakutolani!Pamsana panu!
The deligation is just too big. We are facing hunger in different parts of this country, shortage of medicines in our hospitals. That money could have been used to import medicines and maize. Mapwiya muri metii enyepanapwasi yeeyo. Miano kiri always vanduhli vinyuh koma vala mookipwesa murhima