Email a copy of 'Malawi court revokes bail for murder suspect Ali Kaka' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

21 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Philimon Kaluluma
Philimon Kaluluma
8 years ago

Ambuye agwireni dzanja ananfedwa. Ndipo mkantheni mdyerekezi Ali Kaka komanso ma Lawyer amene amapereka ziweruzo mokondera anthu andalama ali olakwa kuti adziwe Ukulu Wanu. A M E N

makhumula
makhumula
8 years ago

Ali kaka ndi munthu oyipa heve, anatola chikwama atabera boma la amayi 20 million atamamgidwa ndi kasambal. Kaya cashgate yaphonya pati kwape ameneyu.
Amangidwe basi n he wil never become M p in malawi muno.

Man rich
Man rich
8 years ago

Akanakhala mphawi bwenzi ali ku alimande zaka 15 osamusegulila mulandu.chilungamo chili pati?

Decent citizen
Decent citizen
8 years ago

Lawyers without morals only obsessed with making immoral money.If it was your own brother how would you feel about it?Ntchito zinazi muzaatenga nazo matembelero.How would u shield a thug like Ali Kaka?

Decent citizen
Decent citizen
8 years ago

He is a thug.Don’t gloriify murderers.He should be rotting in jail by now.

Mtochi
Mtochi
8 years ago

Selective justice. Why let this murderer free?

ibrahim makwati
ibrahim makwati
8 years ago

Ali kaka dikilani chilango chamulungu chifukwa cho
zikonda mpaka kuchosa moyo chifukwa choimisa galimoto molakwika taonani mulungu akukudikilani

sure
sure
8 years ago

munthuyu mmesa anawomberadi? ngati anapha munthu theres no point kunzungulira ndi nkhani apa…..he did it..

MAPWEVUPWEVU
MAPWEVUPWEVU
8 years ago

PANAKAKHALA KUTI NTCHITO YONYONGA ANTHU ILIPO NDINAKALEMBELA NDIKUNGONYONGA ALI KAKA BASI NDIKUSIYA MALAMULO APANO NDIOPUSA MUNTHU ANAPHA MUNTHU KOMA AKUTI AKUGANIZILIDWA KOMA ZOWONA MUNTHU AMENEYU AKHALE OVUTIKA PALIPONSE AKUYENDA

Gule Wa Mkulu
Gule Wa Mkulu
8 years ago

In first place how can any sensible court grant bail to s murderer? It beats common sense. Kodi ma court a Ku Malawi mwatani?

Read previous post:
I’m absolutely falling apart – Gwanda Chakuamba

Malawi veteran politician in retirement from front line politics, Gwanda Chakuamba, has said he is living a destitute life due...

Close