Email a copy of 'Malawi court sends to jail hubby for undressing wife in public' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi court sends to jail hubby for undressing wife in public' to a friend
This year's annual celebrations for tribal grouping, Mulhako wa Alhomwe, will take place on Sunday at their headquarters, Chonde in...
Akazi, mukuchulutsa kugawitsa ma password. Panopa mwa akazi okwatiwa onse okangomufunsira walora.
Five months only? This moron should rot in jail!
Fandumu, boma ma hips ntchafu…waonetsa kwa anthu. …hahaha…
how can you do this to your own wife??????????? f*************k.
its pathetic for a man to undress his wife in public. I am sure those clothes did not come from her cousin, but maybe from her secret lover. Though this might be the case, no need to shame your wife on public. He would have been given a Hardee punishment and not mere 5 months.
Anamuchita bwino mahule kuchuluka mdziko muno. The only bad thing was asking his kids to be part of the crowd otherwise i see no problem. Why do you think some of us are singke? We are fucking too many married women mpakana kumatipempha kuti tidziwameta mabvuzi. Why keep cattle when you are getting free milk?
Ngakhale patapezeka umboni kuti zachoka Ku chibwenzi, is it Worthy kuvulana? kumbukirani ” amene sanachimweko ayambe kugenda” why can’t you forgive? 5 months its a joke
Kaya zovala za kuchibwenzi kaya ndani, kumuyalusa pagulu sikuthetsa nkhani. iwo alibe nyumba? izi zikanachitikira ku nyumba kwawo, ngakhale mwamuna akanawotcha zovala panalibe mlandu. ndi zawo zakuchipinda.
5 months is a joke. The man even called her children to see the mothers naked. Mother and children will never forget that. After serving a few months this evil man will come our laughing whilst the victim is scarred for life. No no.
Thupi la mkazi mmene limawopyera ungaliyaluse poyera. Amusekera komanso akalifunanso thupi lomwe waliyalusali. akamuchitako matanyula kumeneko. akamutulutsa akafikire kwina.
Mkazi samachepa