Email a copy of 'Malawi cuts spending on patients meals in hospital' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi cuts spending on patients meals in hospital' to a friend
Reverend Chimesya Phiri is not new to sexual controversy that threatens his vocation. The Prison Chaplain for Blantyre Synod of...
@Kanda usakwiye.To me bola kuti mankhwala azipezeka.For the meals ma guardian asova
Apa ndakwiya asaaaaa
aKalilani akukana chani nawonso. mayesa zadutsa muoffice mwawo. thats the foolishness of Malawian leaders. If it was somewhere they cud be shot dead for being foolish.
use the money from sale of MSB Bank
Boma iloooooooooooo!!!!!! Munthu kudya kamodzi mchipatala nzoona izi????. Wena amachita ngozi pamsewu, munthu wakuchitipa umpeza ali Kuchipatala ku Dedza, amene angadzampatsile nthochi ndani aliyekha munthu mumanja mwa boma???????
iwe peter nkhani yonseyitu ili pa mutu pako uli kuti kodi?nanga ukutinawo chani nkhaniyi?koma iwe maso mphenya oti tikuvoteranso mu 2019 ndilibe zikusokonekera mphwanga.nanga anthuwa akafa ati akuvotere ndindani. mphwanga samalira kwambili usogoleri wako
stupid mapwevupwevu govt
Inenso siukundigwira mtima.
Azipatalanu musamatipusitse timaona majumbo a zakudaya mukupita nawo kunyumba. mwachulutsa zotengatenga. pano tiyamba kuika maprivate companies aziphikira ma patients azidya bwino. wina alira ndi zimenezo tikufufuza.
I say empty all the freezers and fridges in Parliament and State house and feed those that deserve it and put all the politicians on a diet. It will do them a lot of good to be little thinner. Save millions in overseas health care as well.