Email a copy of 'Malawi govt backtracks on hospital user fees' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi govt backtracks on hospital user fees' to a friend
The Malawi Confederation of Chambers of Commerce and Industry (MCCCI) has asked the government to speed up the process of...
Zch Dental Keep It Up,mwakhwana Ngakhale Room Yachepa.
Comment;ANTHU A KU ZOMBA TINAZOLOWERA ZA ULERE.KULIPIRA NDALAMA KU CHIPATALA KUTHANDIZA KUTI MANKHWALA ASAMASOWE.CHIPATALA CHA MANO CHA KU ZOMBA NCHAPAMWAMBA,MA DOTOLO AKE NDI ODZIWA NTCHITO KWAMBIRI,KOMANSO AULEMU.PITIRIZANI KUTITHANDIZA NDALAMA ZILIBE NTCHITO BOLA CHITHANDIZO,ZIKOMO.
I ATTENDED THE SKIN CLINIC @ KCH . WHAT IS THE EXACT BY PASS FEES? IS IT MK1600 OR MK1000? THE GR I WAS GIVEN SEEMED A FAKE ONE NOT THE ONES THAT COME FROM GOVERNMENT PRINT WITH SOFT PAPER. PAYING SERVICES BOTH 2 QECH & KCH LEAVE A LOT TO BE DESIRED AND NEED RIGOROUS REVAMPING IF THEY ARE TO BE USE FRIENDLY BUT ALSO ATTRACTIVE. AVOID BY PASS GATE PLEASE AND ISSUE REAL GRS
Very sad. Where are the systems to manage this.
Koma chamba ichi ndiye Chihana chamukhuza nchani
Yes Hospital free but prescription of medicines should be charged and should be bought anywhere at the pharmacy!! we may have drugs in hospitals for direct for doctors to treat admitted patients.
Mbambadi m’theradi MULUNGU kundisunga ndi moyo voti yanga simukanadzaiona ndithu akhakhakha a DPP inu
Atulooo Inuu!
You are playing with Peter’s votes my friend , shupiti , mzimu wa Chasowa ukuona, ndipo ulipo
Number 1 and 3 I think DPP simukuidziwa. Musadzayerekeze kuichepysa mungadzalire chidodolido. Mungofunsa anthu atatu okha, JB, Jessie and Lazarus akuuzani kuti akatakwe amenewa a china Dausi ndi mitengo yaminga, Kweni mkati ndi super league. If you ask JB, akuuzani kuti akayang’ana ku Malawi amangoonako mdima okhaokha chifukwa chomwe analakwitsa iye nchapafupi. Kuchotsa D pa DPP ndikupanga PP basi. Ndichokhachotu basi koma eni akewo samadziwa! Meaning PP without D = failure!
This is what the government said all along, so what do you mean by backtracks? It is as usual the half cooked journalists in Malawi who report things wrongly. Put it simply, if you live in Ndirande and go to Ndirande clinic, you will get your services for free, however if you decide on your own not to go to Ndirande but instead to QECH, you will pay a bypass fee for bypassing your local health facility. QECH is a referral hospital, you need to be referred to there!