Email a copy of 'Malawi govt launches probe on missing presidential palace property ' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

29 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Gimbogo
Gimbogo
9 years ago

Mipando ndi mbale zimenezo zili kuno kwa Goliati bwerani mudzatenge

Chimphyanya
9 years ago

Ngati aliko kutundu wao apaseni. Nkhani ndiyonena kuti nonse simunakonzekere kuti wina achoka ku statehouse nkulowako wina.

Komanso inu nanunso simunatcheke kodi kuti apa pakusowa katundu nkuzatiwudza lero zoona. Are u serious.

Makwinja
Makwinja
9 years ago

Koma abale mpaka katundu kumasowa ku state house president Ali komweko? Pamenepa tiziti waba ndani? Koma dzikoli linali pa ntambasale,mpaka katundugate ku nyumba ya boma? JB be serious please, Dausi tafwanthamula chingerezi chija umuuze jb kuti ndiwazibwana, walowanso libolonje.

MABVUTO MALIKEBU
9 years ago

MALAWIAN PIPO

Kangandiwamba
Kangandiwamba
9 years ago

Anaiwala pant ndy akatenge.mumupatse mpata kwinaku atibwezere mbale ndi mipando

Kanyimbi
Kanyimbi
9 years ago

Mpakana kuba mbale? Amangwetu.

innocent
innocent
9 years ago

amalawi muziwona nkhani zolemba mu news pliz mpaka mbale zoona.mwandichititsa manyazi ndithu kuno ku southafrica.tumani munthu azatenge 20 dozen of plates & medical stuff.

Aliphee
9 years ago

muzani akupanga lecture ku londone school of economics inu mumalo moyendetsa ziko mukupanga probe katundu waboma kodi akati boma ndi chani mungatiyankhe .Anankhumwa palibe or chimodzi chokuyanjani pangani timanyazi pangóno chifukwa mukuyambazi simuzikwanitsa. komanso muyembekezere state funeral posachedwapa

mbuje
9 years ago

Katunduyo anasowa liti ?Kodi sipamakhala ma handover mukamasinthana nyumba kapena office ? Amene anamupatsa ntchito yoyang’anira nyumba imeneyi ( state residences) akuti chani za katundu yemwe mukuti akusowayo ? Bwanji osakawona ku Ndata Pajatu winayo anachita kuthamangitsidwa atalephera chisankho ndiye mufufuzane nokha nokha pajatu nonse ndinu akuba, zazii

abwana
abwana
9 years ago

alomwe onukha kamwa ndi kulogolora zopusa..Nakhumwa leave JB alone.

Read previous post:
JTI discusses tobacco future with Malawi economists

One of the world’s largest cigarrete manufacturers JTI says embracing and harnessing Malawi’s newly adopted Integrated Production System (IPS) of...

Close