Ngati kasambala mumampatsa belo Aniva walakwanji not to deserve belo. Give him belo or else am coming to pick him up. Simuzamuonanso . Anthu akuba ma billion nkuwapatsa belo koma osauka wa hire yo chinda alive mawu. Osakawamanga makolo amene amampatsa ndi kumupanga hirer bwanji. Zengani mwachilungamo ana akupasidwa AIDS pa stereo mungoyangana.