Email a copy of 'Malawi is wrong, Prophet Bushiri trashes ‘Satanic’ slurs on AFRICCI' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

125 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Pida
9 years ago

Ma Jesuits pa ntchito yawo tsopano. Akudzera mwa a khristu a Sunday kuti paumaliro adzazunze a christu a pa Sabata la Yehova. Aloreni, avomerezeni a AFRICCI anuwo, mudzazindikila last minute kuti a khristu a Sabata la mu baibulo aja amanenadi zoona satana atakulikwilani. Chiyambi chakudzakakamiza anthu tonse kumadzapembedza pa Sunday. Posachedwa manthu wa mavuto afika. Ngakhale andichotse sukulu, andichotse ntchito, andidule manja sindidzanena kuti Sunda ndi Sabata, ayiiiiiiiiiii! mpaka kukadutsa mtambo wobilieilawo.

Pida
9 years ago

Chiyambi cha THE NATIONAL SUNDAY LAW. owerengawe khala maso. Well educated people, very intelligent people but they have no wisdom, kumvera kusocheretsedwa. Kumvetsa chifundo ma educated savages pa mau a Mulungu Yehova. Mulungu atseguleni maso anthu anu akuonongeka chifukwa cha kusadziwa.

kabefula
9 years ago

Inu azibusa a ma pente, tamaphunzitsaniko ma members anu za kuti machismo ndi ati, kuchita bwino pa uzimu ndi kuti osati kumangoti ayi Mulungu atikondera atipatsa chuma, tipeza mabanja, ayi tikwera pa ntchito, madalitso ochokera kwa Mulungu amabwera munthu akaleka uchimo, amene amabwera mu ma pente churches wo amachokera kwa satana chifukwa ndinu ambiri a inu ndinu ma hule, ma rejects ndiyeno mumajoina mipingo imeneyi kuti kuti satana akupatseni mwamuna, mkazi, ndalama za pansi pa Nyanja. Mulungu akutsanulilani chuma bwanji uhule uli thooooo, ma mimi mu church, kuvina dance wachikunja mu church. Muzingosanza dzithumwa, dzinjoka dzomwedzo satana ndikumakupatsani nsato muli… Read more »

Movettie c.p phiri
Movettie c.p phiri
9 years ago

Amalawian pz pz pz stop talking about men of God or any other person ndipo the truth of the fact is mukamali kuyakhala zamunthu WHAT DO YOU GAIN? Pz pz pz thats bad!

Tikonda
9 years ago

Amalawi amalawi tadzukani dziko lathu litukuke, mulungu akufuna kukuthandizani, inu mukuti ndi sataniki, zizindikiro ndiye zaoneka zokwanira, ansinga amasulidwa, odwalanso achilitsidwa. kodi ufumu wa satana ungaziukire okha, yesu anaonanso zoterezi.

Favour
9 years ago

Malawi must be delivered from the spirit of poverty. She hates people who were destined to raise the country because of jerous. Prophet Bushiri’s vision must be supported and Malawi will never be the same again.

Wilmuw
Wilmuw
9 years ago

If it’s like that juliusphil then God must be vey poor, yet the bible says ; heaven and earth belongs to Him 1 chronicles 29:11 and Jesus said all that the Father has are mine and Roms 8:17 days we are joint heirs with Jesus. My brother let’s pray that our mind is renewed from poverty mentality.

Makala
Makala
9 years ago

Malawian malawian malawian,wabwino azakhala ndani,ngakhale ine ndinabwela kuno ku southafrica,ndakhala zaka folo,osapeza ntchito yabwino,lero Allah(mulungu)wayankha yapezeka ndayamba kumanga nyumba akuti ndalowa SATANIC,kkkkkkkkkkkkkkkk,,malawi tinazolowela kuvutika,ndiye izi sizodabwitsa ,vuto ndi atsogoleli athu,akanga ndiwamba,kkkkkkkkkkkkkkkk,am wishing yu al the best Mr president of Africci,plz help ure pourest country malawi,,maybe we can change,bola owapatsilawonso muzawonesese,hahahahahahahaha

Thitherward Wendo
Thitherward Wendo
9 years ago

Until our education system improves, we shall remain vulnerable to confidence tricksters like Bushiri and his kind.

KING SOLOmon'S WISDOM
KING SOLOmon'S WISDOM
9 years ago

I FOR ONE I TRUST THIS MAN OF GOD.I DO ATTEND HIS SERVICES AND AM PROUD TO BE ASOCIATED WITH HIM.I LIVE A LIFE OF FAVOR SOON ,PPLE WHO KNOW ME WILL BE SURPRISED AT THE FINANCES COMIN MY WAY.GOD BLESS THIS MAN .GOD HAS NO LIMIT

Read previous post:
Lilongwe Technical College introduces sports day

True to the wise saying that goes- All work and no play makes Jack a dull boy, Lilongwe Technical College...

Close