Email a copy of 'Malawi itches for win over Mozambique as South Africa, Zambia booted out of Cosafa Cup' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi itches for win over Mozambique as South Africa, Zambia booted out of Cosafa Cup' to a friend
Some traditional leaders in Lilongwe Mapuyu North constituency have expressed concern with the poor working relationship between the legislator for...
Listen pliz zoti chimozi ndi chamangwana are nt strong enough to be the flames coach and call kinah phiri ine ndikususana nazo, kinayo anali ponpa zinamukanika kale komanso tangoganizani pakathawi kochepa komweka koma taonani team yaphanvu yomwe atulusa madolowa and ife tikumwa wankaka, tikunva kukoma and lose ya mozambiq chisakhale chiphinjo kwa ma coaches anthu iyayi ngati zili choncho nde kuti RSA, Zambia ndi Ghana naoso awathamangisa ma coaches bcoz naonso aluza, just imagn malawi lose to RSA 2-1 in friendly bt MWI managed to beat RSA in cup game this means an inprovment is there so pliz pliz pliz… Read more »
Zimachitika kuluza please call back kinnah if we are to develop in football a malawi ndi kinah team yinali boo tandivekeni please
Nde tiziti bwanji tsopano,taluzatu mxiiii!!
Malawi has played well but why timangodzichinya tokha? Flames were supposed to win the game. Anyway it happens. Nanga titan pot zachitika kale. Am very worried as a malawian mulungu udziwa kutonthoza atonthoze a malawi.
Malawi has played well but why timangodzichinya tokha? Flames were supposed to win the game. Anyway it happens. Nanga titan pot zachitika kale. Am very worried as a malawian mulungu udziwa kutonthoza atonthoze a malawi.
Chimodzi and Jack are not fit to be flames coaches. They must be booted out. Cosafa and Afcon which is stronger and bigger? If Young failed to advance in cosafa, can he achieve in afcon? Tribalism and nepotism have got effects in any development. Kinnah is better off than Young. ‘Jacket sapisila’
Zambia 2 Malawi 0
South Africa 2 Malawi 1
Now Zambia and South Africa they are all OUT now Malawi what will happen?
We owez love Malawi’koma osamangozichinya tokha.
Go Malawi
Tangokhazikani mitimapasi. Tingodikila 95mins basi. Coach plz osamangobwebweta zamatimu ena ayi dikilathawi yatimu yako kuti uwone zithabwanji ndipomwe uyambekulalatano kwakoko. Osamangodyandalama zosaoneka ntchotoyake ayi. Kulibwino ndalamazo azithandiza anthu osauka