Email a copy of 'Malawi JBFI partners with UK Rotary Club, rolls out ‘mobile’ water barrels' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi JBFI partners with UK Rotary Club, rolls out ‘mobile’ water barrels' to a friend
Police in Karonga the northern border of Malawi has arrested Jimmy Sichone, 29 of Malemia village in the traditional authority...
Anthu mumkaseka amai kugawa ngombe ndi mbuzi. Lero mmidzimu mbizi ngome zubelekana mkumapeleka mkaka. Iwo a makaka a chimamga ,chimangacho kulibe angodya wokha phwando. Keep it up JB F
mzilibwino mupitilize mama
abambo ena ake andebvu zawo akaona chonchi basi kumangokodzedwa okha, kubwebweta JB. Mmawa tingomva atuma kansilikali kawo ali yankhulani kuti JB anapha auje, linalo ali nenani kuti kuli zithunzi za ma camera, kupita kunja kuphwando kumene kukanika kudya mtima pha pha pha chifukwa cha nzimayi okuti ali phee iye kwake ndikungoganizala anthu obvutika basi. Mulekeni mzimayiyu simungamulande chimene Mulungu anaikiza mwaiyeyu.
Great idea
Booooma ilooooooooo!!!!!!!!
The are the most trusted children of JB and they misled her Bin Time. Running a government is a serious business and not family matters.
Iwe Roy, wavala chani kodi? I dont think muslim clerics will like that when you aont one of them
aaah!! icant trust her anymore,why is she afraid of coming back home..akudziwapo kanthu za cashgate ameneyu.
Gooood job mama. This is development. Lucky are those living in flat areas, they will use the barrels. Very many poeple will enjoy. Pliz, mama, continue searching for other better methods.
Muliyenda mwanu muphindulira aMalawi.
Amene sakuzifuna azisiye. Koma ine munditumizire 10 on sale order more for sale in shops. Nzabwino zinthu izi.
Anthu like JB atakhalapo ambiri bwezi dzikoli litatukuka.