Email a copy of 'Malawi leader appoints new boards: Full list including CSOs leaders' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi leader appoints new boards: Full list including CSOs leaders' to a friend
As insecurity problem rages on in Malawi, a group of armed robbers in the capital Lilongwe beat the security detail...
Ma appointees enawa ndima hule akawononga ku ma parastatals. I wish akanamapanga background check before appointing them. I know Frank Mbeta who has been appointed pa board ya ku MACRA. He is married but right now he has gone to South Africa for a holiday with a girlfriend, Keiko Msusa. Yemweyo amanyengana ndi Pachalo mpaka the two girls fought for him at TJ’s bar.
ifenso maudindowo tikuwafunatu
Congrats amnzanga amene tasankhidwa. Tigwire ntchito basi.
am just surprised kuti mmene maina achulukiramu dzina lathu ife amang’anja palibepo.
Ife ndi amene tagenda ku boma eti?
Dean Josaya akufuna abwenzeretse zomwe ayiwonongera Epac FC, awone kusintha amwene.
Putting party organising secretary at the hem of ESCOM is a recipe for financial mismanagement of the already struggling parastatal. We don’t want to see ESCOM vehicles taking people for party functions please! I hope your long stay in US was not in vain.
Mpaka Abigail !!!!!! Boma ili nde ndilamasanje ndithu
FR Andrew Kaufawo muwawuze asiye kuchitila nkhanza ogwira ntchito awo ku TV Luntha ndi Montfort Media komwe atolankhani amagwila ntchito mwamatha chifukwa cha nkhanza za mkulu ameneyu. Ndipo samayenera kukhala mu board ya MACOHA
Congratulations guys. I can only wish you well
Kaya zanuzo but congra Namba!