Email a copy of 'Malawi man arrested for indecent assualt on boy, 13' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

14 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
osman usu justin
osman usu justin
9 years ago

Utsogoleri wamathanyula

zanga phee
zanga phee
9 years ago

Koma ameneyu bwanji?ma D 7 onsewa sakuwaona , osangopita kwa kachere bwanji ?akathandizidwe, ku wishes, Hip Hop,Town house, kumphasa, kapena ku full dose..ngakhale kwa masapula alipo akazi ongoyenda yakali yakali, umenewo ndi Mwikho mamwene, akaseve basi ku ZOMBA MAXIMUM PRISON.

siyabonga nhlapo
siyabonga nhlapo
9 years ago

alomwe alomwe noooooooooophiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiyaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa!!!!!!!!!!!!

MELINDA
MELINDA
9 years ago

BOKO HARAM yonseyi,ena kumachita kudikilirana kuli kufuna kunyowetsedwa mpaka ena pamzele,ndithu zokuonera galu wachisika iwe.paja kwanu mkuti?

Utiyankhulitsa pakhundu,koma dziko lilidi m’manja mwa agalu eti!!!!!!!!

muduleni zinthu mbuzi adamupatsa ambuyakezo kuti nkhanza zimenezi asadzachitirenso wina kapolo wa chilomweyu

saukani wakuda
saukani wakuda
9 years ago

Awone kiama ameneyo abwere LL tidzangomuchotsa katundu wakeyo. Just to curb his libido

Rich North
Rich North
9 years ago

Zonsezi ndi APM,there is more to come

Mbatata 4011
9 years ago

Ufiti Eti,,,,,ameneyo Amusekele Ku Ndende De Whole Of His Lyf

Batchala
Batchala
9 years ago

Nyere zanji zoukira pa mwamuna mnzako?

musisipala
9 years ago

Rubish and not fit for human consuption. This devil must go to hell

chikondi chinansi
chikondi chinansi
9 years ago

Koma ndichani a Malawi ufiti eti akazi osewa sakukanaso ameneyo alangidwe basi

Read previous post:
Malawi loan seekers suffer higher interest rates, says Standard Bank

Standard Bank Group has revealed in its most recent release that higher interest rates and tough economic conditions in Malawi are...

Close