Why is everyone a bit chubby for an international model figure. .nsima is a carbohydrate which gives more carolies if u can’t burn the carolies they will turn fats and farts girls..advice. Well done anyway
bax
9 years ago
Ana amumpanda @ their Level Best kukulira pacinena !!!!!!! Babylon Can’t Study Rasta::hh!!! Hell BOund Business!!!
Nesfold
9 years ago
Ngat muli mndalama za phwamwamwa osakawa thandiza abale ndi longo avutika ndi madziwa bwanj,, ndithu maliseche akhale okopela alendo? Mw ukunka kwan?
Kavuluvulu
9 years ago
Zoputsa basi.
Bauleni
9 years ago
am concerned.you want girls nakedness attract tourism.dirty money
YOLANDA
9 years ago
what a devilish manner
kingstone
9 years ago
Napezambo wanga. Kuphatankhuphata baa.
zanga phee
9 years ago
Malawi wa lero at its best, Satana watenga ulamuliro onse , opezetsa ndalama kudzera kuwonetsa umaliseche wa atsikana, koma atsikana amenewa ali ndi Makolo awo kapena awatenga ku orphanage, shame on you girls , komanso makolo mukawona mukuti chani, kunjoya kumeneku eti, come 2017 , if not carefull these girls will be no more, sinanga akuwonetseratu pakhota nyani mchira, what next, maplain basi ithyoke ithyoke. with HIV EEEEEEEEE, Ulendo ulipo.
Mabvi pamatako, let’s face it, we are no longer living the Chilembwe era, things are changing and we have to go with the floor. Girls be proud of yourself, show us what you’ve got.
Why is everyone a bit chubby for an international model figure. .nsima is a carbohydrate which gives more carolies if u can’t burn the carolies they will turn fats and farts girls..advice. Well done anyway
Ana amumpanda @ their Level Best kukulira pacinena !!!!!!! Babylon Can’t Study Rasta::hh!!! Hell BOund Business!!!
Ngat muli mndalama za phwamwamwa osakawa thandiza abale ndi longo avutika ndi madziwa bwanj,, ndithu maliseche akhale okopela alendo? Mw ukunka kwan?
Zoputsa basi.
am concerned.you want girls nakedness attract tourism.dirty money
what a devilish manner
Napezambo wanga. Kuphatankhuphata baa.
Malawi wa lero at its best, Satana watenga ulamuliro onse , opezetsa ndalama kudzera kuwonetsa umaliseche wa atsikana, koma atsikana amenewa ali ndi Makolo awo kapena awatenga ku orphanage, shame on you girls , komanso makolo mukawona mukuti chani, kunjoya kumeneku eti, come 2017 , if not carefull these girls will be no more, sinanga akuwonetseratu pakhota nyani mchira, what next, maplain basi ithyoke ithyoke. with HIV EEEEEEEEE, Ulendo ulipo.
Chikhalidwe chikuwononga,,, tiyeni zizitere tiziwona mbinazo zili pa ntunda,, zili bwino osati kumangowonera zolaula kuchipinda kokha