Email a copy of 'Malawi Muslims’ leader under attack over abuse of funds' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

42 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
concerned
concerned
8 years ago

IWE IBRAHIM MAKWATI !!!
IWENSO USATIBOWE APA , OLO UTAMANGIDWA ANGADANDAULE NDINDANI ? ZAZIII

ibrahim makwati
ibrahim makwati
8 years ago

MUSAIWALETU PAJA NDINAMANGIDWA CHIFUKWA CHA SHEIKH UMALI OCHI PANO NDI MANGIDWA CHIFUKWA CHAINU

zaluma
zaluma
8 years ago

I have no problem seeing Muslim stealing. It is part of their legacy Profet Muhamad left. Mtendere ukhale kwa iye

Eagle eye
Eagle eye
8 years ago

Mijomba yaliranso ndi cashgate yawo.Kaya situmizilanapo boko haram pamenepa?He he see koma ziliko pamalawi.

SHAIBU MSUSA
SHAIBU MSUSA
8 years ago

KODI SHEHE SALMIN NDI CHAIR WA MAM MAGALIMOTO AMENE AKUYENDERA ANAGULA NDI NDALAMA ZOCHOKERA KUTI CHIFUKWA ANALI MPAWINSO NGATI INE? THESE ARE THE QUESTIONS WHICH NEEDS ANSWERS
BUT EVEN IT WAS DECIDED THAT SALMIN OR KAWINGA CONTEST FOR CHAIR OF MAM SANGAWINE CHIFUKWA THEY ARE SPENT FORCE. NKANI IMENEYI WAYITULUSA NDI SHEHE JAFALI KAWINGA CHIFUKWA ALIBE CHOCHITA NDIPONSO SAKUGAYILIDWA MA ALLOWANCE KUCHOKERA KU MAM. WINANSO NDI MUSSA CHIMBENDE NTOLA NKHANI WAMKULU KWASILAMU AMENE ALIBE NCHITO KOMA KUMADYERA PACHIKAMWA PAKE AKATIGULISA NKHANI NDI ANA AKE ASIKANA AKAPANGA SELL MATUPI AW
IFE ZIKUTINYASA MUKAMALEMBESA NKHANI ZACHISILAMU PA INTENET CHIFUKWA MULIBE UMBONI WOKWANILA

Bahasa
Bahasa
8 years ago

National chair ndi MR pomwe SG ndi Dr. koma yaaaaaa

Chikuni
8 years ago

Musiye kusokosera pa Radio Islam chifukwa ndinu nomwe amene mukutiphunzitsa khalidwe lonyasali.

Tseketseke Nkholo Sugar

I only know one clean Sheikh Ali Kennedy and he don’t accept nonses. Pray zat Allah intervens and bring peace among fellow Moslem.

Reality wisegel
8 years ago

Paja asilamu mumakonda mapokoso komanso ngondo,tamenyanani tionele nawo kkkkkk

katapwito
8 years ago

SH Idriss MHD mwaiwala zomwe munalonjeza ndimanga Universty Chipatala cha Aslam you evin promised kuti ndibwino kuti muzizakwera mamin bus koma muzasamala chuma cha Asilam today you are driving porsh cars ndinu odala ndyerani Chisilamu mmene mungathere but 1day you wil Answer pa maso Allah sinu nokha ai koma aliyense yemwe chuma chake chikukhudzana ndi ndalama Zachisilam ndiotembeleledwa Masheikh akumalawi chonde chitani manyazi chisilamu mwachidyera kokwanira plz plz tapanganiko zoti mawa ana athuwa azaone kusinthako taonani mipingo ya anzathu moti inu omwe muli atsogoleri a MAM simupanga manyazi ?

Read previous post:
Mponda says money does not buy success: ‘Wizard FC will survive’

Former Surestream Technical Director Peter Mponda is confident that his team now named Wizards FC will do well in the...

Close